Summit Systems

Summit Systems

Share

Summit Systems is a registered Malawian ICT business under the Business Registration Act (No.12 of 2012).

The business focuses on developing and advancing technological solutions that bring people, systems and ideas together to solve real world challenges

30/07/2026
30/07/2026

πŸ”° Mukutsalira ndinuyotu ohoo πŸ₯±

Henewe! Download Voyage Ride today. Izi zomangoti zunguli zunguli pa depot ayi mabwana πŸ™Œ

https://play.google.com/store/apps/details?id=com.mycompany.zobandukaapp

28/07/2026

Kampani ya Summit Systems yaku Lilongwe, yomwe imapanga zamtokoma (ICT) yapanga application ya pa foni yotchedwa Voyage Ride, yomwe cholinga chake ndi kulumikiza madalaivala ndi anthu ofuna kukwera galimoto omwe akupita njira imodzi.

Voyage Ride, yomwe ikupezeka pa Google Play Store, imalola madalaivala kulemba ulendo wawo posonyeza komwe akuchokera, komwe akupita, kuchuluka kwa mipando yomwe ilipo komanso mtengo omwe akutchaja pa mpando. Anthu ofuna kukwera amatha kuona maulendowa ndi kulumikizana ndi dalaivala kuti ayende limodzi.

Kuphatikiza apo, anthu ofuna kukwera amathanso kulemba komwe ali komanso komwe akufuna kupita kuti madalaivala anjinga zamoto ndi galimoto athe kuwapeza kudzawatenga komwe ali.

Pa Voyage Ride palinso malo otsatsa magalimoto a hayala komanso malo ena othandizira kugawana uthenga wa komwe kukupezeka mafuta nthawi ya kusowa kwa mafuta agalimoto ikafika kuti eni magalimoto asamangozungulira-zungulira kusaka mafuta.

Kampaniyi yati application yi ili mu ziyankhulo za Chichewa komanso English kuti aliyese athe kugwiritsa ntchito mosavuta.

M***a kuipeza app yi Ku Google Playstore kapena dinani link ili m'musiyi yomwe ikutengeleni Ku Playstore:
https://play.google.com/store/apps/details?id=com.mycompany.zobandukaapp

24/07/2026

πŸ”° Free advice. We love you πŸ₯±πŸ₯±

06/07/2026

πŸ”° HAPPY BIRTHDAY MALAWI, HAPPY INDEPENDENCE WARM HEART OF AFRICA πŸ”°

10/06/2026

πŸ”° Yafera pamwambatu. Waimanya? πŸ˜‚

Henewe! Download Voyage Ride today. Izi zomangoti zunguli zunguli pa depot ayi mabwana πŸ™Œ

https://play.google.com/store/apps/details?id=com.mycompany.zobandukaapp Mikozi

03/06/2026

Pa Depoti kukukwakwaza ndalama ili yako? πŸ˜‚ Sizoonayi. Download Voyage Ride today!

https://play.google.com/store/apps/details?id=com.mycompany.zobandukaapp

25/05/2026

Mmmm mpkana pamenepo
Book your car with voyage ride. Travell on your terms, stay flexible and actually get the car you actually want

17/05/2026

πŸ”° Call for Car Hire Companies πŸ”°

Voyage Ride ndi zonse mommo! Ma ride komanso car hiring ikutheka. Osachedwa, auzeni omwe alindi galimoto za hayala avunge pa Voyage Ride.

Download Voyage Ride app today!
https://play.google.com/store/apps/details?id=com.mycompany.zobandukaapp

Voyage Ride 17/05/2026

πŸ”° Pena chizungu chimazunguza. Osadandaula! Pa Voyage paliso Chichewa. App yokhayo yomwe ili n'Chichewa. Kwatsala Chitumbuka πŸ˜‚

Download Voyage Ride today:

Voyage Ride

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Ahmedabad?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Address

Box 702
Ahmedabad

Opening Hours

Monday 7:30am - 4pm
Tuesday 7:30am - 4pm
Wednesday 7:30am - 4pm
Thursday 7:30am - 4pm
Friday 7:30am - 4pm