Himalaya General Traders

Himalaya General Traders

Share

We stock safe, efficacious, affordable Himalaya pure herbal products & other health-care products

Photos from Himalaya General Traders's post 16/11/2023
16/11/2023

*CHEBE mankhwala a sitsi*
K9,000 bottle

Chebe air food amapangidwa amapangidwa kuchokera ku Chebe tree ndi zina zachilengedwengati shea butter, peppermint oil, Cocoa butter, Moringa tissue oil ndi zina zambiri.

Chebe hair food amagwira Ntchito pa tsitsi la chilengedwe losathila mankhwala

Ntchito zake ndi;

1. Kukulisa tsitsi ngakhale lokanika
2. Kuthana ndikuyabwa kwa Tsitsi
3. Mudetsa tsitsi
4. Kuchotsa fundu mu tsitsi
5. Kuthana ndi mavuto a kuwuma mmutu
6. Kupangitsa tsitsi kufewa mkubiliwilisa
7. Kuletsa kuthothoka kwa tsitsi
8. Kuthana ndi oily hair

Alipo ku Himalaya Limbe shop komanso madela ena onse timatumidza.

Call or WhatsApp 0884717200

Himalaya Limbe shop ili opposite THE WOOLSHOP kuyandikana ndi Phalombe Hardware building pa Nasho. Apo pali Airtel shop.

*We are here for your health*

Photos from Himalaya General Traders's post 16/11/2023

ANTI-DIABETES TEA *othana ndi kukwera/ kuchuluka kwa sugar muthupi*

Mankhwala awa opangidwa kuchokera ku zitsamba omwe amamwedwa monga tea *amathandiza zonse izi👇 pothana ndi nthenda ya Diabetes;*

1. Kuonesetsa kuti sugar ali wa mlingo oyenera mu thupi la munthu.

2. Kuonesetsa kuti chiwalo chamuthupi chotchedwa Pancreas chomwe chimatulutsa timichere totchedwa Insulin yemwe ntchito yake ndi kuika pa mlingo wa bwino sugar wamthupi, chikugwira bwino ntchito komanso kutulutsa Insulin okwanira.

3. Amasungunula mafuta amuthupi omwe akachuluka zimapangitsa kuti timichere toika mlingo wa sugar wamthupi pabwino tikanike kugwira ntchito yake bwinobwino.

4. Tea ameneyu ampangitsa thupi lizikhala lachangu kugwira ntchito kumbali yochepetsa sugar pamene insulin akutulitsidwa. Matupi ena amafuna Insulin ochuluka kuti ayambe ntchito yochepetsa sugar wamthupi ndipo tea uyu amathandiza kuti matupi ayambe kugwira ntchito mofulumura ngakhale insulin ali ochepa.

5. Tea uyu amathandiza kuti chiwindi chizichedwa kupanga komanso kutulutsa sugar opita muthupi. Choncho akasungidwa munjira ina ndipo osatulitsidwa sugar muthupi amakhala mulingo wabwino.

6. Kuchapa impsyo kuti zizigwira bwino ntchito yake ndipo zisamasungebe sugar yemwe amayenera kutuluka muthupi munjira ya mkozo. Zikachitika zimenezi sugar amathuluka kuchepa muthupi mosavuta.

7. Tea ameneyu amathandizanso kuonesetsa kuti sugar akuchoka wambiri muthupi pochapa thupi lonse.

*Ntchito zonse za tea ameneyu zikuthandiza kuthana ndi mitundu yonse ya Diabetes*
1. Diabetes 1
poonetsetsa kuti Insulin akutuluka okwanira muthupi kuti agwire ntchito yake yoika sugar pamlingo wabwino.

2. Diabetes 2
Ponesetsa kuti njira zonse zothandiza kuti sugar akuchoka muthupi komanso kukhala pa mlingo wabwino zilibwino.

*Kagwiritsidwe ntchito kake*
1. Ikani teabag imodzi mmadzi owira kwa mphindi zokwanira 5. Imwani

Bweledzani kuika teabag yomweyo mmadziena imwani ndipo kachitatu phwatsulani teabagyo muike zonse zili mkatimo mmadzi

Photos from Himalaya General Traders's post 16/11/2023

HYPERTENSION TREATMENT TEA *otsitsa BP*

Tea uyu opangidwa kuchokera ku zitsamba *amathandiza zambiri*👇 pamoyo wa munthu maka kwa omwe ali ndi vuto la kuthamanga kwa magazi;

1. Kuthandiza kuika kathamangidwe ka magazi pa mlingo oyenera.

2. Kuotcha kutsungunula mafuta ammagazi komanso omwe amapedzeka munjira zodutsa magazi omwe akachuluka amachepetsa njira zodutsa magazi ndipo magazi kumadutsa movutikira BP kukwera.

3. Kusitsa vuto la magazi omwe akuthamanga kwambiri kupotsa momwe zimayenera kukhalira.

4. Kuthandiza impsyo kuchotsa madzi komanso michere yotsafunira muthupi zomwe zimakoledzera kuthamanga kwa magazi muthupi zikachuluka.

5. Amathandiza Kupewa kuti mchere komanso madzi atsachuluke muthupi

6. Kuika pa bwino mafuta amuthupi kuti asakhale pa mulingo oyambitsa mavuto.

7. Kuchotsa zoyipa zomanga pachifuwa zopangitsa munthu kukanika kupuma bwinobwino

8. Kuthana ndi ululu wapachifuwa, mmalo mokumana mafupa komanso kuphwanya kwa thupi zomwe zimachitika pamene magazi akuthamanga mopyola muyeso wake mu thupi lamunthu.

9. Amathandiza ndipo ndi ofunikiranso kwa anthu omwe akuvutika ndi mphumu kapena Asthma.

10. Kuthandiza Kupewa mavuto onse a mtima, kufa kwa ziwalo komanso kuundana kwa magazi muubongo.

11. Tea ameneyu amathana ndi mavuto amuubongo obalarika komanso kuyiwala.

12. Kuthana ndi vuto la kukanika kupedza tulo.

13. Kuchapa chiwindi

*Anthu omwe akuyenera kugwiritsa ntchito Tea ameneyu*
1. Anthu omwe ali ndi sugar ochuluka muthupi
2. Anthu omwe BP yawo ili yokwera
3. Anthu omwe akutsowa tulo
4. Anthu omwe ali ndi mavuto amtima
5. Anthu omwe ali ndi mafuta ochuluka muthupi

*Kagwiritsidwe ntchito ka Tea uyu*
Kutenga teabag imodzi kuika mmadzi owira kwa 5 minutes kenako kutakasa kumwa madziwo. Pangani izi mobweredza kawiri

Kuphwatsula teabag kutenga zonse zidali mmenemo kuika mukapu kumwanso zonse osataya kulikonse.

Kumwa Kamodzi or kawiri patsiku.

*Mtengo*
K17,000 pack ya 20teabags

Mankhwala amenewa apedzeka ku Himalaya

Photos from Himalaya General Traders's post 16/11/2023

*Vuto la KUTUPA/KUKULA KWA PROSTATE / enlarged prostate* 0884717200

Prostate ndi kalabala kenakake komwe kamakhala muthupi pansi pa chikhozozo polumikidzana ndi chida cha abambo.

Prostate imatulutsa madzi omwe amathandiza umuna ochokera ku mabattery abambo kuti uziyenda mosavuta.

Prostate imathandiza kwambiri pankhani yamoyo wa uchembere wa bambo.

*Kutupa kwa prostate*
Abambo ambiri omwe afika dzaka 50 zakubadwa amakumana ndi vuto la kukula kwa prostate ndipo imakula or kutupa kufika pa size ya ndimu.
Izi zili choncho chifukwa choti pamene bambo akukula prostate imakhala ikukula.

*Zizindikiro za enlarged prostate*
1. Kukanika kukoza, kukanika kumalidza kukoza or kukoza mopyola myezo
2. Kufuna kukoza pafupipafu
3. Kukoza mwazizi
4. Kuotcha or kumva kupweteka pokoza
5. Kumva kuphweteka pokozera umuna nthawi yogona ndi mkazi.

*Kuthana ndi mavuto vutoli*
1. Sinthani moyo wanu wa tsiku ndi tsiku monga kupewa kumwa madzi ochuluka panthawi yomwe mukupita kogona.

2. Kumwa mankhwala ochepetsa zizindikiro za kukula kwa prostate komanso ophwetsa prostate yomwe yakula kapena kutupa.

3.Surgery. Azibambo omwe vuto lawo lakula kwambiri palibepo kuchitira mwina koma kuwachita operation kuti kuwalowetsa pipe yothandiza kuchepetsa mavuto odza kaamba ka vutoli.

*Kuopsa kwa vuto lakukula kwa prostate pankhani yakukwanitsa kupereka pakati*
1.Kukula kwa prostate kumaseka njira kuyimitsa mikozo komanso umuna kudutsa kuti zitulukire koyenera zomwe zimakanikitsa bambo kupereka pakati.

2.Mankhwala enanso othandiza kuthana ndi vuto lakukula kwa prostate alinso ndi kuthekera koyambitsa vuto lokanika kupereka pakati.

3. Chiyambi cha Prostate cancer. Abambo ambiri omwe ali ndi vuto la enlarged prostate amapedzeka ndi vuto la prostate cancer.

4. Kulephera kugwira bwino ntchito kwa chikhozozo, impsyo komanso kudwaladwala matenda amunjira yamkozo.

*Mankhwala chokera ku zitsamba othana ndi vuto la kukula kwa prostate*

K17,000 Himplasia tablets

0884717200 Himalaya Limbe shop pa

Photos from Himalaya General Traders's post 18/08/2023

*Mankhwala opangidwa kuchokera kuzitsamba ochilitsa ma ulcers/zilonda za mmimba komanso kuthana ndi acid ndi mavuto ena a mmimba* 0884717200

Mukuvutika ndi maulcers kapena kuti zilonda za mmimba?

Kodi mukumamva ululu kaamba kakuchuluka kwa acid mmimba?

Nanga mukumageya zonunkha zomwe zikumveka ngati heartburn kumaotcha pamtimapa?

Kapena mukadya chakudya mukumamva kupweteka mmimba?

Mankhwala opangidwa kuchokera ku zitsamba a Himalaya Yash*timadhu tablets amapha tizilombo tonse toyambitsa zilonda za mmimba amachepetsanso acid kuti asamatiluluke oyambitsa mavuto mmimbamo.

Zikatero kumakhala kuchila kwamaulcers komanso kutha kwa kumva kuotcha kwa pamtima ndipo ululu onse omwe mumamva mmimba umatheratu.

Mankhwala alipo Blantyre mu Limbe komanso timatumidza madela ena onse zimafika pamene munthu wagula.

Bottle k15,000

Komanso pali tea othana ndi mavuto ammimba maulcers, kupweteka kwa mmimba, gas, kufufuma kwa mimba, kutsegula mmimba, kutsowa kwa chilakolako cha zakudya, kutsagayika kwa chakudya

Superherb stomach care tea k17,000

Thandizidwani lero pa # iyi 0884717200

Himalaya Limbe shop ili OPPOSITE THE WOOLSHOP next to Phalombe Hardware pa Nasho.

*Himalaya Wellness Malawi; Here for your health*

Photos from Himalaya General Traders's post 17/08/2023

*HIMALAYAN PINK SALT / MWENJE SALT*

*1kg* @ k10,000 (Retail), k7,500 (order)

Mchere uwu ndi otsiyana ndi michere ina chifukwa suupeleka mavuto alionse muthupi lamunthu.

Ndipo uli ndi ubwino komanso umathandiza zinthu zambiri monga;
1. Kuika Sugary muthupi pa mlingo oyenera

2. Kuika kathamangidwe ka magazi muthupi pa mlingo oyenera

3. Kuthandiza kukhala ndi chilakolako chogonana ndi munthu

4. Kuthandiza kuti munthu usamakule mofulumira

5. Kuonjezera mphavu muthupi

6. Kuika madzi amuthupi pa mlingo oyenera

7. Kuika michere yamuthupi pa mlingo oyenera

8. Kuthandiza kuti zakudya zopatsa thanzi zizilowelera mosavuta.

9. Kuthana ndi ziwengo, msungu komanso mavuto ena apakhungu

10. Kuthandiza thanzi la ubongo

11. Kuthana ndi mavuto onse akapumidwe

12. Kuthana ndi kupweteka kwa mmimba panthawi yopanga period

13. Kuthandiza kuyenda kwa magazi muthupi

14. Kuthandiza thanzi la impsyo

15. Kulimbitsa mafupa

16. Kuthana ndi vuto lotsawa tulo

17. Kubwedzeretsa madzi muthupi

18. Kuthana ndi fungo la mkamwa komanso lapakhungu.

19. Kuthana ndi makandantchembere

20. Kuthana ndi zikang'a

21. Kuthana ndi msungu za mkamwa

*Nchere umenewu ndi 💯 wachilengedwe mulibemo zoonjezera zilizonse ngati mumichere inayi*

*Ndipo uli ndi michere komanso zinthu zina zofunika pamoyo wa munthu zopitilira 80*

*Kagwiritsidwe ntchito*
1.Umagwiritsidwa ntchito monga nchere ulionse kuika mu chakudya

2. Kuika mu madzi osamba molingana ndi vuto lomwe mukufuna kuthetsa

3. Kufwenthera molingana ndi vuto lomwe mukufuna kuthetsa.

4. Kuika mkamwa kuchukucha molingana ndi vuto lomwe mukufuna kuthetsa.

Ulipo ku Himalaya Limbe shop

Tili pa Standard bank roundabout OPPOSITE THE WOOLSHOP, next to Phalombe Hardware.

Helpline; 0884717200 / 0998033132

*Himalaya Wellness Malawi; Here for your health*

Photos from Himalaya General Traders's post 07/01/2023

*VUTO LOYIWALAYIWALA / KUBALALIKA / MEMORY LOSS*

Vutoli ndi kuyiwala kodza mosadziwika bwino. Munthu amatha kuyiwala zinthu zangochitika kumene kapena zakale penanso zonse.

Vutoli limatha kukhala lakanthawi kochepa kenako kapena loyambiranso komanso lanthawi yaitali molingana ndi chomwe chayambitsa vutolo.

*Mayina ena avutoli;*
Forgetfulness, Amnesia, Impaired Memory, Loss of Memory, Amnestic syndrome, Dementia-memory loss, Mild Cognitive impairment- memory loss

*ZOYAMBITSA*
1. Kukula
2. Kuvulala kwa ubongo
3. Zotupa zamuubongo
4. Pochidza Cancer
5. Kusafika kwa oxygen okwanira ku ubongo
6. Kuvulala kwa mutu
7. Nthenda yamuubongo
8. Kudwala nthawi yaitali
9. Surgery
10. Stroke
11. Kudzadza kwa madzi mu ubongo
12. Nkhawa
13. Kubalalikabalalika
14. Mowa
15. Kugwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo
16. HIV/AIDS
17. Kugwiritsa ntchito mankhwala nthawi yaitali
18. Kuchepa kwamavitamin B muthupi ( Vitamin B1, Vitamin B12)

*Chitsamaliro chapakhomo*
Munthu yemwe akuyiwalayiwala amafunika chitsamaliro chachikulu.

1. Kumawaonetsa zinthu zosavuta kudziwa, nyimbo komanso zithuzi zodziwika mosavuta.

2. Kumawalembera nthawi yoyenera kumwa mankhwala or kuchita chinthu chilichonse chofunika.

3. Ngati munthuyo akufunika chitsamaliro tsiku lililonse komanso thanzi lawo sililibwino pakuyenera kuyamba chitsamaliro chapakhomo chitsamalira odwalayo tsiku ndi tsiku.

*Mankhwalawa opangidwa kuchokera ku zitsamba*

Tili ndi mankhwala opangidwa kuchokera ku zitsamba a *Himalaya Mentant tablets*

Mankhwalawawa amathandiza kuthana ndi vuto loyiwalayiwala, kupangitsa munthu kuphunzira zinthu mosavuta, kukhala wachidwi, kuthetsa kubalarika komanso kuthandiza kubwezeretsa nzeru zamuubongo.

Botolo la 60 tablets @ K12,000.

Himalaya Limbe shop ili pa Phalombe Hardware mu building ya Masha-Allah Merchandise Mart ground floor room ITN28. Opposite Standard Bank

Helpline; 0884717200 /0998033132

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Limbe, @ Phalombe Hardware, Masha-Allah I. T. N Nathanie Merchandise Mart, Ground Floor Room # ITN28. Opposite Standard Bank
Blantyre

Opening Hours

Monday 07:30 - 17:00
Tuesday 07:30 - 17:00
Wednesday 07:30 - 17:00
Thursday 07:30 - 17:00
Friday 07:30 - 17:00
Saturday 07:30 - 17:00
Sunday 09:00 - 03:00