ZILI KUNO MW
About helping others to get what they need
Bambo anu ankagulisa Makala k*t muphunzire,lelo ndinu Nsilikali mukulanda makala a makolo azanu bola inu mudaphuzira ayi zikomo
Vuto lopanga chibwezi ndi munthu oti anaonapo Kamuzu,lelo ndi izi mwadwalika
2 -0 Malawi ik*tsogola
1- 0 Malawi ik*tsogola
Pano zilipati ndi ajawo munkalumbira pa Pamaso pa abusa ku church k*ti muzakhala nawo moyo wanu wose?
Kod mwawauza kale a X aja k*t pano mukadalibe munjira?
ZILI KUNO MW About helping others to get what they need
Ukudwala kma akuuza k*t uchire ugonane ndi X wako ungatani?
Click here to claim your Sponsored Listing.