The Bond Tv Malawi
Student journalist at Malawi instutute of journalism. Content creator. Poet
28'|
Injury Update!
Thuso Ng'ambi is injured and is being replaced by Isaac Chair Kaliyati.
Wanderers 0-0 Silver
ππ The Bond Tv Malawi
5'|
It's underway here at Zomba Stadium.
Wanderers 0-0 Silver
The Bond Tv Malawi
With Fabrizio Romano β I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!
21/05/2026
The Bond Tv Malawi
MAlawi News HUB
MPHEKESELA
Inu mukutipo bwanji pa nkhaniyi?
Muuzeni Emmie Deebo Ali Olandilidwa Ku Get Money Clique π°Recordsβ¦ Ma Conditions;
(1) Ma Video Ake Tizikapanga Shoot Kunja.
(2) Room Yogona Kunjako Uzikagona Room Imodzi Ndi The Biggest Mkulukuta Hip Hop. Uku Ndikuchepetsa Budget Ya Ndalama Za Malo Ogona.
(3) Ugulilidwa Galimoto La New One Koma Siyikhala Mu Dzina Lako Kufikira Miyezi 9 Utaonetsa Ma Results A Mbewu Ya Bwino.(Nyimbo Yomvera Mwana Wa Mamuna Olo Wa Mkazi Ndi Nyimboso Yabwino)
(4) Nyumba Ngati ili Ya Rent Uzilipilidwa Kuphatikiza Kugulilidwa Ma Groceries A Mwezi Onse !!
(5) Kuno Unjoya, Usalala, Unenepa Ndipo Sizinaoneke Ndipo Adani Ako Amva Pain !!
By Management!!
21/05/2026
Otsatira timu ya Arsenal ku Salima yomwe ndakatswiri achinkho cha mdziko la Mangalande chaka cha 2025-2026 akonza ulendo wandawala kaamba kotenga ukatswiri wa ligiyi.
Wapampando wa komitiyi a Mike Mwawa ati iwo akonza ulendo wandawalawu pofuna kuwonetsa kukondwa kuti timuyi yatenga chinkhochi patapita zaka zokana 22 asanatenge chikhochi.
A Mwawa apempha anthu okonda timuyi m'bomali kuti akhoza kubwera ku ulendowu kuti azawonetse nawo chimwemwe chawo chomwe chidzayambira pa Community Hall kuthera ku ubunthu Lodge komwe kudzakhale made madyelero.
Ndipo mmodzi mwa anthu okonda Timuyi m'bomali a Grecious Amiton ayamikira ganizo la komitiyi popanga mphwando kaamba kachipambanochi.
Wolemba Ousman Kaliati
The Bond Tv Malawi
Copied from Times 360 Malawi
19/05/2026
Oky Arsenal ββπ―π―π―ππ
19/05/2026
Team ya manchester city yafanana mphamvu ndi team ya Bournemouth lelo pa masewero amu English premier league
Bournemouth inayamba kumwesa chigoli chake choyamba zomwe zinabweletsa chimwemwe pa team yi
Izi zinali chomwechi mpaka mphindi zonse nkutha. Pamenepo kunaonjezeledwa phindi 6 kuti masewelowa athe.
Apa ndipomwe manchester city inamwetsa chigoli chawo kupangitsa kuti mpira uthere draw.
Zatelemu arsenal ndekuti ndima champions a 2026 English premiur league
The Bond Tv Malawi
19/05/2026
MAMA YANGU
GOAL!!!
Bournemouth 1 manchester city 1
The Bond Tv Malawi
π Bournemouth Vs Man City
67'
Arsenal fanz still praying harder
Bournemouth 1-0 Manchester City
The Bond Tv Malawi
It's half time now Bournemouth 1 manchester city 0
19/05/2026
MAMA YANGU
GOAL!!!!!!!!
39. Kroupi gives Bournemouth the lead.
π 1-0 π©Ά
Click here to claim your Sponsored Listing.
Address
Blantyre