Zokonda amayi

Zokonda amayi

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zokonda amayi, Blantyre.

20/09/2023

Tili ndi anyamata awiri amene akusaka ntchito ya u driver
Kwina kulikose komwe ingapezeke at akafkako
Ndye mwabwana ndi madona ngat ntchito muli nayo alembeni anyamatawa avutika kwambiri
Code license C1
Code license B

12/09/2023

Ma fans follow this page Blackview Mobile Malawi

12/09/2023

Hello admn. Pls hide my ID.... Ineyo ndi abwela kuno ku South kuzasaka ndine mzimayi WA Ana awiri kumudz ndinasia mwana mmodz kuno kuli mmodz.... Ndikugwira ganyu panapezeka mamuna kukambirana za banja ndipo zinatheka timakhala bwino bwino mosaziwika bwino mamuna anasitha zochitika. Kufufuza ndapeza zoti Ali ndi mkaz akupanga nae chibwez. Mamunayu akumangindilalatira kuyakhula mosakhala bwino chonde azimayi ndithandizeni mzeru. Ndipange nae chani Mamunayu kapena mkaziyu.... Chonde okhawo Ali ndi maganizo othandiza si zonyozayi... Zikomo

12/09/2023

Moni azimayi Ine ndizimayi wa zaka 22 ndili ndi mwana modzi ndikufuna ntchito kwa amene amveleko Pena pake andiuzeko chonde azimai Kaya yanyumba olo ya shop ndikhoza kugwila ndimakhala ku lilongwe chonde azimai ngat mungamveleko mundiuzeko azimai number yanga ndi imeneyi

09/09/2023

Onesan love popanga follow page iyi👉👉 BlBlackview Mobile MalawioBlackview Mobile MalawiaBlackview Mobile Malawi

09/09/2023

Ma fans tyen uku Blackview Mobile Malawi tkadye 50 k

07/09/2023

Morning ma fans
Follow this page Blackview Mobile Malawi mukadye ma fafandede ama unints

25/04/2023

Kusadzwa mkufa komwe mumadzwra chan amuna kt mkaz wathra plz help musandnyoze

13/01/2023

Hie post for me

Kodi Patricia Kaliyat ndngamupeze kuti

08/01/2023

THANKS FOR 10 K FOLLOWERS

06/01/2023

Hie, post for me ndne tsikana wa zaka 23 ndmakhala ku Blantyre chirimba ndmafuna ntchito ina iliyose kaya yogulisa mu shop kaya reception ndzina zotero ngat ilipo tikodolen please tavutika kwambiri 😫🙏🙏💓

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Culinary Team

Attire

Telephone

Address

Blantyre