Elegant Wig Gallery
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Elegant Wig Gallery, Beauty, cosmetic & personal care, Lilongwe, Likuni, Lilongwe.
09/01/2026
09/01/2026
Ma Brazilian bundles wo bwelesani ndikupangileni wig yokongola mamie
Ndili ku Blantyre chilomoni, kindly follow my page ladies.
25/12/2025
Azanu akutchena ndi ma wig a 100% abwino
Follow our page mutipase order yanu
Tikupangireni wig ya smart, muzioneka bosslady
Blantyre, Chilomoni.
20/12/2025
Follow my page if you're in Blantyre and mukufuna ma wig a smart, aka ka 100% zatengeni kasananthe Chilomoni
03/12/2025
Amene mukufuna ma wig abwino ngati ndavalayi,, tasamukila ku Blantyre, Chilomoni
Tipaseni order tikupangireni mitengo yosiyanasiyana.
Sizochita kuntha ma week 3 days imakhala yatheka.
Follow my page kuti uziona tikapanga post
25/11/2024
Available zatengeni Likuni Lilongwe
K45000 only
Brazilian hair wig
13/11/2024
Zatengeni ku Likuni Lilongwe
K26000 yokha
0884326404
01/11/2024
Ku ukwati,ku church,ku graduation kumafunika ka wig kabwinoko abale tipaseni order muzitchena
Price ndi K26000
Location Lilongwe likuni
Number 0884326404
Don't forget to like/follow our page muziona ma wig abwinowa
22/10/2024
Inuyo kutchena ai?Ndipezeni Lilongwe likuni
Whatsapp number
0884326404
Musaiwale kupanga follow and like our page muziona ma wig a smart wa
11/10/2024
Tatipasani order yo akasi inu tikupangileni braided wig yokongola ndipo yosavuta kusamala.
Ndili pa likuni p***a mitengo imatengela style,size ya closure ndi katalikidwe
Starting from K24000 going up
Mufuna yotani
Just like our page kuti muziona ma wig amene Ali available
06/10/2024
Ma wig anthu timasoka ndi machine ndipo amakhala olimba komanso okhalisa
Tiyeseni ulendo uno muvaleko wig yabwino
Amene mukusunga ma hair bundles tipaseni tikupangileni ma wig abwino
Tapangani like/follow us muziona ma post anthu tikaika ma wig abwinowa
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe