Small wifey
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Small wifey, Health/Beauty, Lilongwe.
I got over 100 reactions on my posts last week! Thanks everyone for your support! π
Hey guys mwaona mwamaliza e simwaiwala bc
09/07/2025
Eti abale
Komatu Small Wife naye a Cosoma anakamuganizirako
Model emwe Chaka chino wapezeka mu nyimbo za oimba ambiri otchuka ku Malawi kuno Small wife anthu akuti naye akuyenera kumuganizirako for spicing up the industry
Chabwino a Cossoma sizikuwakhunza Koma oimba Omwe mwagwira naye ntchito Ndipo mwalandira ma Million muzizimuseni Small Wife
08/07/2025
Mwandisowa e kma mwapanga kale follow?
05/07/2025
Muli kt ndilowa live 12 koloko pa lunch ticheze π₯π₯π₯π₯
Ati kodi ulibe zochita zina aaaaaa pangani follow tikumane 12 ba
05/07/2025
05/07/2025
Alamu anu akt moni π€£π€£π€£
Morning
03/07/2025
Duwa lanu lipangeni follow πΈπ
02/07/2025
Hy g**z koma mukupanga follow?
01/07/2025
30 June........ follow my page g**z
Click here to claim your Sponsored Listing.