Mtolankhani Opanda Chisisi

Mtolankhani Opanda Chisisi

Share

📰 Mtolankhani Opanda Chisisi. Choonadi chathu, mawu athu, nkhani zathu.
🔎 Timafufuza • Timafotokoza • Timanena zoona.

Photos from Mtolankhani Opanda Chisisi's post 22/08/2026

Galimotoya mtundu wa Minibus yagwa pa Thabwa pomwe imachokera ku Blantyre kupita ku msanje.
Anthu ochuluka athamangira nawo ku Chipatala cha Chikwawa.

Source: Zodiak

22/08/2026

Akutero graduate wa ku UNIMA🤣🤣👇

"Mu nyengo imene ena amona ngati tikukokomeza koma ayi ndithu

Ma yearo nonse akuwidani 😂"

22/08/2026

Sad news💔👇

Copied and pasted

First year, first Semester Students, Catherine Mvula from Mzimba watisiya atawombedwa ndi Galimoto pa Ginery Coner masanawa when she was crossing kuti akumane ndi Bambo Ake omwe panthawiyo amachokeera ku Mzuzu kuzamupasa Zofunikira...

Rest in peace Catherine💔🙆‍♀️

22/08/2026

Even ma supporter sakuvetsabe💔👇👇

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Website

Address

Lilongwe