Kamteteka page

Kamteteka  page

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kamteteka page, Health/Beauty, Box 37, Livingstonia Mission.

19/02/2026

Mklu ameneyu ndi JB zikumveva kuti akufuna ku joiner MCP wamutulika muthalika, malangizo kupita kwa JB chakwera sanaiwale kuti unkamunena ma battery ndipo kinena mwachidule zilingati wabiba ku toilet kenako ukupita kukasetela mtengo wa kankhande kunkhalango Mr JB musaiwale kuti MCP simapanganika kumvukilani chilima zimene anamupanga, komanso wina aliyese amene amati akanyoza chikangawa party kenako ndikujoina amaphedwa, zikuoneka kuti JB ukufuna pofela, amati pofera salambula koma JB walambula

06/02/2026

🚨‼️THOM KAPEN PEPA‼️🚨

Which song is the best between PEPA and THOM 🙌

Mbali yathu ife THOM nde song koma pepa verse ya akulu wo aaaa or mwna waku primary atha kulemba bwino😩

06/02/2026

Real Gatramiran
👊🏿❤️🙌🏿❤️

06/02/2026
06/02/2026

Eeeeeh ayi zikomo kwambiri 🙌🙌

06/02/2026

Carabao Final yilipo...

Arsenal Vs Manchester City

06/02/2026

Azising'anga and Ma Fake Prophet..
Ichi Chipatseni Ganyu wina Simuzakhumudwa 😂😂😂

06/02/2026

driemo x ronaldo x messi

06/02/2026

What are your top 3 favorite songs from Makadi?

Comment👇🏽

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Livingstonia Mission?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Box 37
Livingstonia Mission