Nkamwini wathu

Nkamwini wathu

Share

Research and Commentators One God believes

25/04/2026

True or false?

23/04/2026

Mmh

20/04/2026

Real meaning ndrama ziri paminga

08/04/2026

Okondeka anga mwa Allāh khulupirira ndipo chikhulupiriro chili mkuchita zomwe Allāh walamula ndi kukwaniritsa.

Zovetsa chisoni timati Takhulupirira koma swalaah sitiswali, Zakaah sitipeleka, mwezi wa Ramadhwaan sitisala kudya. Ndipo sitiziletsa kuzithu zoletsedwa kumangoyendera ine ndi Silamu ndinakhulupirira basi kukhulupirira uku kulibe mphindu lililonse pamoyo wa munthu, ndipo ndikuzipondereza kwakukulu.

Allāh akunena kuti:

وَأُدْخِلَ الَّذِينَ آمَنُوا وَعَمِلُوا الصَّالِحَاتِ جَنَّاتٍ تَجْرِي مِن تَحْتِهَا الْأَنْهَارُ خَالِدِينَ فِيهَا بِإِذْنِ رَبِّهِمْ ۖ تَحِيَّتُهُمْ فِيهَا سَلَامٌ.

"Ndipo amene adakhulupirira ndikuchita zabwino, Adzalowetsedwa kuminda yomwe pansi Ndi patsogolo pake mitsinje ikuyenda, Adzakhala m'menemo muyaya mwachilolezo cha Mbuye wawo. Kulonjerana kwawo m'menemo Kudzakhala: 'Mtendere!'
Suurat Ibraahim 14:23.

قُل لِّعِبَادِيَ الَّذِينَ آمَنُوا يُقِيمُوا الصَّلَاةَ وَيُنفِقُوا مِمَّا رَزَقْنَاهُمْ سِرًّا وَعَلَانِيَةً مِّن قَبْلِ أَن يَأْتِيَ يَوْمٌ لَّا بَيْعٌ فِيهِ وَلَا خِلَالٌ .

"Auze akapolo Anga amene akhulupirira Kuti apemphere swala ndikupereka zina Mwazomwe tawapatsa, mobisa ndi moonekera Lisanawafike tsiku lopanda (chithandizo Cha) kudziombola ndi (chithandizo Cha) ubwenzi.
Suurat Ibraahim 14:31.

Ndipo anafutsidwa Mtumiki wa Allāh (ﷺ) zinthu zomwe munthu angachite kuti akalowe ku Jannah, Abu Abdullaah Jaabir mwana wa Abdullaah Al-Answaariyy Mulungu asangalale nawo akufotokonza kuti:

أَنَّ رَجُلًا سَأَلَ رَسُولَ اللَّهِ صلى الله عليه و سلم فَقَالَ: أَرَأَيْتَ إذَا صَلَّيْتُ الْمَكْتُوبَاتِ، وَصُمْتُ رَمَضَانَ، وَأَحْلَلْتُ الْحَلَالَ، وَحَرَّمْتُ الْحَرَامَ، وَلَمْ أَزِدْ عَلَى ذَلِكَ شَيْئًا؛ أَأَدْخُلُ الْجَنَّةَ؟ قَالَ: نَعَمْ". [رَوَاهُ مُسْلِمٌ]."

"Munthu wina anafunsa Mtumiki wa Allah (ﷺ), "Nanga bwanji ngati nditapemphera mapemphero okakamiza (swalaah za Faradhw), kusala kudya (mwezi wa) Ramadan, kuona kuti ndi lamulo, ndikuona kuti ndi lamulo, osachita china chilichonse (cholensedwa) kupatula pamenepo? Kodi ndinga

26/03/2026

😂

26/03/2026

😂😂😂

25/03/2026

2002 - 2008 Tatumikirapo ndithu

24/03/2026

Vetselani Miyambo yabwino umu!

24/03/2026

Let's support our parents

Photos from Nkamwini wathu's post 10/03/2026

Wapeza Nkazi Wapeza gold

10/02/2026

Mvelaniko aka

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Machinga?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Machinga
Machinga