Chiko b

Chiko b

Share

Two boys ♥️♥️♥️ mum's love

02/08/2025

Page not found.

28/07/2025

Mzimayi wina anataya mwana wa khanda pa mwala atamuveka ndi kumukutira bwino dzulo ku extension 75 ku Polokwane kuno ku South Africa mwanayo akuti amalira usiku onse Koma anthu oyandikira amaona ngati ndi mphaka Koma kutacha analipeza khandalo lili poteropo lili moyo Koma litazizidwa kwambiri

(English translation) A newborn baby was found well dressed and placed on top of a a stone and slept overnight yesterday the incident happened at extension 75 area, Polokwane. 😭💔

Some members of the community thought it was always a cat that was crying and when they listened carefully they found out that it was a baby that was crying because of the cold they reported the matter to the police and they are investigating the baby is alive.

28/07/2025
Photos from Chiko b's post 28/07/2025
Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Mwanza?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Mwaza
Mwanza