Mkaika CCAP

Mkaika CCAP

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mkaika CCAP, Health/Beauty, Mkaika ccap box 36 chia nkhotakota, Nkhotakota.

John 14:24-31 (NIV) - Anyone who does not love me will no | YouVersion 19/04/2026

By Mr malengesa

John 14:24-31 (NIV) - Anyone who does not love me will no | YouVersion Anyone who does not love me will not obey my teaching. These words you hear are not my own; they belong to the Father who sent me. “All this I have spoken while still with you. But the Advocate, the H

19/04/2026

📖YOHANE14:27

Photos from Mkaika CCAP's post 19/04/2026
19/04/2026

Ambuye 'naitana 'ne:
'Dzapumulire kuno,
Tsamira mutu, mwana 'we,
M'chifuwa mwanga muno."

2 Ndabwera kwa Ambuyeyo:
Wolema, wachisoni;
Anandipulumutsako,
Nakondweretsa ine.

3 Ambuye naitana 'ne:
"Ndipatsa anthu madzi.
Wotopa ndi waludzu 'we,
Dzamwere moyo kuno."

4 Ndibwera kwa Ambuyeyo,
Ndamwera madzi awa;
Laleka ndithu ludzulo,
Tsopano moyo wadza.

5 Ambuye naitana 'ne:
"La dziko ndine Dzuwa,
Yang'ana Ine, kwacha 'we,
Wachoka mdima uja."

6 Ndayang'anira Mbuyeyo,
Ndapeza Dzuwa langa
Londiyendetsa bwinolo
Pa njira yonse yanga.

19/04/2026

May Manda ndakatulo.taitle (safuna ma existing yaweh)

19/04/2026

Women's choir

19/04/2026

Chibvumbulutso choir

19/04/2026

Sunday school choir

19/04/2026

Grace of God choir

19/04/2026

Betsaida choir

19/04/2026

Lero lino m'bale wanga,
Ndilo dzuwa lakukoma;
Talandira Mpulumutsi
M'mene ali kuitana.

2 Lero lino m'bale wanga,
Usazengereza ayi;
Ngati ulandira Yesu
Lero, udzachita mwayi.

3 Lero lino ndi labwino;
Moyo wako uli nawo;
Pena m'mawa umwalira,
Udzatani mlandu wako?

4 Lero lino m'bale wanga,
Lapa mtima, lapa tchimo,
Yesu adzakulandira,
Ukapempha lero lino.
5 Ndiwe mlendo lero lino,
Mvera ndikupempha iwe;
Yesu Mwana wa Mulungu
Akufuna ndithu iwe.

6 Inde, lero lino Yesu
Aitana inu nonse.
Landirani Mpulumutsi,
Musazengereze konse.

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Nkhotakota?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Mkaika Ccap Box 36 Chia Nkhotakota
Nkhotakota