King Bakali Mtchana

King Bakali Mtchana

Share

Hard working yield success

19/09/2025

Kodi muli mbali itiyo munyngo ya unofficial yi

19/09/2025

tiguleni

Photos from King Bakali Mtchana's post 29/01/2025

Ophunzira wa sitandade 7 Memory Kanyika, yemwe amadziwika pa masamba a mchezo kuti Ndaziona, komanso yemwe amayendetsa tsamba lake Ken B Wazakena, lero anayitanidwa kuti akawonekele ku polisi.

A Wazakakena omwe tayankhulana nawo mphindi zapitazi, ati anapita ku polisi yaying'ono ya Kabula chama 3 koloko masana, kenaka anawawuza kuti apite ku polisi ya Wenera.

Koma iwo ati, akuchokako kumene usiku uno, kupolisiko, koma sanawawuzebe chomwe amawafunira. A Wazakena ati, awawuza kuti abwerenso mawa, kuti adzamve zomwe apolisiwo akuwafunira.

Ophunzira wa sitandade 7, Memory, amadziwika ndi nthabwala zomwe amachita pa Facebook komanso pa masamba ena a mchezo.

(by InnocentKumchedwa-Lilongwe;01/28/25)

17/01/2025

*Apolisi mdziko la Zambia amanga Mayi wazaka 51 Sylvia Mutoba Kalaba pamodzi ndi ana ake kaamba koti mnyumba mwawo mwapezeka thupi lakufa la mwamuna wawo yemwe wakhala akusowa kwa zaka pafupifupi ziwiri.*

Malingana ndi nyumba ina yowulutsa mawu mzikolo ya Diamond, yati mchimwene wa malemuyu Emmanuel Kalaba wauza apolisi kuti iwo ngati akubanja akhala akusakasaka m'bale wao ndipo mayiyu amakaniza anthu kufika ku nyumbayi.

Zadziwika kuti malemu wa ndi a George Kalaba, omwe anali osewera mpira wakale wa timu ya Zanaco.

Malingana ndi mneneri wa apolisi m'dziko lo Rae Hamoonga, wati kutsatira kafukufuku iwo anakwanitsa kupita ku nyumbayi komwe anapeza khomo lotseka koma anthu ali mkati, ndipo atalowa anali odabwa kupeza thupili litasala mafupa okha pa k**a m'chipinda china.

Ndipo pakadali pano, apolisiwa akusunga muchitokosi mayiyu Sylvia Kalaba, azaka 51, pamodzi ndi ana ake anayi omwe ndi Natasha, 19, Sandra, 22, Wendi, 27, komanso mwana wina wa zaka 15 ndipo kafukufuku ali mkati pofuna kuziwa zambiri pa nkhaniyi.

16/01/2025

Mukathyoka khosi mudxinamidzila ngoziπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

16/01/2025

Room ya student wa unima,, komatu shaaa

28/11/2024

With 265 ENT MAG TV – I just got recognized as one of their top fans!

20/11/2024

Dzafika povuta sopano

10/10/2024

Koma gyz mzikhalako seriousπŸ™„πŸ€”πŸ€”

10/10/2024
Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Namiwawa
Zomba