Ungwazi
Nasanganya wazinthu
kuchimpwilikiti
kumpanipani kwenikweni
10/09/2026
Sad news💔
Ku South Africa dera la George Munthu wamwalilira kuganyu anamuyitana ganyu azinzake akuti amakumba pipe then kenako analowa kuti a kiline pipe yo then nthaka inasweka nkuwakwirila wina mutu umawoneka koma agondwewa anali pansi panthaka ndiye zinavuta kuti awapulumutse ndimmene wafera mzathuyi
Mzimu wa Victor Gondwe ukause mtendere💔🕊
Malume akangoyamba ubusa apa🙌🏾
Follow Ungwazi
Kodi ukuso mukuwelenga ma weeding dress?
Congratulations Onesmus
25/08/2026
A President a ku USA Donald Trump, wati mbendela ya US isitsidwe ku US kwa one week popeleka ulemu kwa Dolly Parton, yemwe wamwalira lero ali ndi dzaka 80. Mzimu wake ukause mtendere💔
Anayimba nyimbo ya
It's too late
Coat of my colors
Silver and gold
Think of Love
Jolene
Ndinyimbo zambiri💕💕
21/08/2026
Ndiangati omwe sitimaziwa kuti alindimwana wasize yimeneyi?
Happy happy blessed birthday to Ovilera Longwe
💕💕
Follow Ungwazi
Mwana wa 8 years kucapetown wazipha ndichingwe cha pajama (chovala chogonera) chomwe waziphera sichikuziwika mwana wanzathu wakuMalawi Ambuye atonthoze makolo ake💔💔
Follow Ungwazi for more news
Ataluza ma vote ahonorable akuzambia anaganiza zokachotsa denga lomwe lili theka landalama zawo😝😝
Follow Ungwazi for more
Ana onse kulakwa pa school vuto ndi ana mwina aziphunzitsi?
Follow Ungwazi
British man baby dadie wa Vanesa Pink anapita ku court zitapezeka kuti Mwana amene adali naye siwake after ma DNA asisi athu anamukoloweka British man 🙌🏾
Follow Ungwazi for more
Mbolanso Bwanji
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Mzimba
......