Fight Club: Healing Together
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Fight Club: Healing Together, Pretoria.
Certified Life Coach| Narcissist Abuse Survivor|
Mental Health Advocate|
Seasoned Public Health Expert |
Sickle Cell Warriors| Motherhood|
Truth-Seekers| Cycle-Breakers|
Let's have the hard conversationsβΌοΈ
ππππππ« πππ₯π ππ©π’π¬π¨ππ π!
Nkhani ya Mama & Dada.
π¬
Anonymous: Ndipeleke second chance kwa baby daddy?
Ine ndi mamuna wanga tinasiyana tili ndi mwana mmodzi wa chaka chimodzi. Tinasiyana chifukwa choti amandimenya komanso amapanga zibwenzi kwambiri nde ine ndinatopa.
Nditamuuza k*ti ndatopa ndipo ndikupita kwathu sanapepese olo kundinyengelera mulimonse anangoti chabwino. Ineyo ndinkaona ngati tikhala pansi tikambilana zomwe zikulakwika. Nditaona mmene mwini wake anayankhila ndinadziwa k*ti uwu ndi mtunda opanda madzi ndinalimba mtima nkuchoka. Timangokhala limodzi koma sitinapange ukwati nditachoka ine ndinabwelera kwathu kwa mayi anga. Ndinali ndi ka business kanga mowawidwa momwemu ndinangolimbikila nkuzitolera pano ndimakhala pa ndekha ndi mwana wanga.
Nkhani ndi yoti mamunayi titasiyana sanachedwe anapeza mkazi wina komanso ndimava zambiri zokhudza ndi zibwenzi zina zomwe amapanga. Pano akamabwela kuzaona mwana wayamba kumapepesa ati wazindikila kulakwa kwake. Tsiku lina anabwela akumwa mowa wake anakhala mpaka kudya nafe dinner kenako ak*ti watopa nkupempha k*ti angogona nawo.
Kwa ine ndinaona ngati munthuyi akungondamizila k*topa akungofuna kudya katundu. Mind you ine nditachoka anayamba kukhala ndi mkazi wina uja koma pano ati anasiyana. Nde ine zoti agone ndinakana ndinamuuza azipita kwao.
Koma wakhalira kundivutitsa ma message ati tibwelerane mkazi yemwe amamukonda mmoyo wake ndi ineyo wazindikila mochedwa
Ineyo mtima unalimba koma ti ma feelings kukhala ngati tilipobe chifukwa zayamba kundisokoneza pena ndikumaona ngati amandikondadi. Koma nkaganiza komwe ndachokelaku nde mantha akumandigwila.
Nk*tani pamenepa? Ndipeleke mwayi wachiwiri kwa baby daddy kapena ayende?
Anonymous: Heartbreakππ
Thanks for giving me an opportunity munthune ndikungokhalila kulira nkhani yanga ndiyaitali koma ndiifupikisa
Am 29 in age am single mum ,she is a girl 7 yrs old std 3 munthune I was working on a certain company koma ntchito naima panali zifukwa Zina ,,, komaso ndakhala pa relationship kwa 3 yrs after ndi bambo amwana titasiyana mwana wanga Ali Chaka chimodzi ndipamene ndinapeza nzangayu ndipo anali work mate wanga zinthu zinali bwino sinapezepo vuto linalililonse mpaka Chaka k*tha mpaka tinalowa Chaka chachiwili ,, muchaka chachiwili kunabwela abwana athu kuzatipangisa meeting it's when anafika paiyeyo kulankhula zoti inu ndiye musapange zibwana ndi ntchito ma pampers anadula ine nadzidzimuka chifukwa sanandiuzepo chilichose chamwana ndipo I got mad after that meeting ndipamene ankafotokoza k*ti anachimwitsa nkazi ndiye pot kwao ndinkapita basi nangot ndiyek*t mene zimakhalila anthu amachimwitsa after 4 months k*ti ndipite kwao anayamba ma excuse ine kumadabwa ataona ndakwiya he came kuzandiuza k*t munthu anamuchimwitsa uja Ali kwao akusowa pokhala ndimwana I was confused namukwiila nasiya kumulankhulitsa tinatha mwez koma zikundiwawa komaso munthuyu ndinkukonda kwambili k*tengela so ndimene iye amandikondela ndinakhala mwez winawo ndiye there was certain guy ndimacheza naye kwambili naye anali oti banja lake linatha ankandifuna basi tinayamba ngat chibwez pamene paja koma mtima wanga unali ukondabe munthu wina uja komaso anali akupepesa the new guy I Ali long distance relationship ada aja anabwelaso tinavomeraso kupusa kwake anatiuza palibe chilichose pakati paiyeyo ndi nkaziyo ife tinavera k*tengela ndimene timakhalila timangoti basi zoona mamuna anasamuka kupita kulilongwe koma every weekend amakhala Ali kunyumba kwangwa kukasungu ine kumangoti zinthu zibwino koma wina uja kumangocheza naye sitinkakumanasoi uyu atabwela kachiwilimu anapanga hack phone yanga ndipo anapeza chat ya ine ndi nzanga timacheza zokhudza ma relationship ndipo nzanga was comparing k*ti bola winayu banja lake linatha than this person uyu akuchedwetsani he got mad mpaka he ended relationship koma ine ndamene ndinapepesano mpaka we get back again nkati mwandime kumapeto kwachaka nayamba kulandila ma phone kwa nkaxi wake uja kulandizana mawu zosaenda zija mpaka munthu uja anapita kwao timakhala mu relationship ija koma things want the same last week we went ku lake we had fun zobhebha zija from there I went kwao Sunday munthu anayamba kulira kufusa Ati he is feeling like he is loosing me ine how palibe kumandipanga praise you are a good woman everything is good paiwe but nduona ndupanga loose chinthu chabwino nangomusiya Monday he drop me home lachitatu ndangoona chi long message praising me for being a good woman to him koma ak*ti I loss his trust popeza ma message amene tinkacheza ndi nzanga aja oti I have someone oti alibe nkazi
Ndabalalikilatu 3 yrs wasted time πππndikungolira panopa napanga block palipose and he asked me k*t why ndapanga block pamene wapanga end zinthu ,,mybe he was the one amandipasa bzy ine ndimangodikila nthawi ndipange move on
It's long story zambili ndaduladula koma ndilimbitseni mtima azimai ndikungokhalila kulira ine
Happy Sabbathππ½
Pepani ngati mwatumiza anonymous in the past few days. I have been busy. Life happens.
Will post your stories this weekend.
Matelazi a lero.
Episode 2 ya Better Half Lero madzulo 6pm!
Anonymous: Ga ga ga mulibe mnyumba!
Please hide my ID. Ndimafuna anthu pa group andithandizeko.
Ndinakumana ndi mamuna wanga chibwenzi changa cha nthawi yayitali (5 years) chitangotha. Ndinali ndidakali mubheart break. Iyeyo anali banja lake litangitha atangopanga divorce. Nde tonse tinali mobalalika nde chibwenzi chathu chibali chonocheza kwambiri timakhala ngati tik*tonthozana. Koma chomwe chinandidabwits apa chibwenzi nchok*ti munthuyi samaginsa zofuna kugona nane. Mu chaka choyamba tinapanga s*x just kamodzi. We never discussed this issue at all komanso poti tonse tinali obalalika basi zimangodutsa choncho. Mpaka tinayenda kimodzi for 2 years and we were very close. We. Got married chala chachitatu...we still disnt have much s*x and we never talked about it.
On our wedding night munthu analibiletu excitement ya s*x. Ine ndinkati mwina tatopa. Days passed, he didn't show any sign yofuna s*x. Ku honeymoon kuyesa kumugwila nothing happened. Ine ndinakanika k*ti ndifunse koma for the first time ndinaganiza k*ti ndakhala ndikupanga ignore nkhani yofuna kwambiri. Titabwelako ku honeymoon ndinayoyambitsa nkhani ya s*x koma he took offense and ananena k*ti kodi banja nde k*ti ndi s*x basi?
I felt embarrassed kenako basi ndinasiya kufunsa masiku nkumapita ga ga ga mnyumba zero. Ndinakanika kupilira kensjo ndinalemba email k*tifunsanso nkhani ija sanandiyankhe.
Then tsiku lina bdinayitambutsansi nkhani ija anandiwuza k*ti di mbali yake.
2 years married pano koma I am starved.
Zikatele mumatani? Help me.
ππππππ« πππ₯π: ππ©π’π¬π¨ππ π
Padangokhala with Brenda Dzanja....
Tiyeni tiyeni tiyendele limodzi nkhani ya Mama ndi Dada.
27/05/2026
My people Fight Club. .shout with powerπ
Tiyamba kuwulutsa nkhani ya ππππππ« πππ₯π (Mama & Dada) lero at 6pm.
Tiyeni tiyendele limodzi.
It's Movie TimeβΌοΈ
ππππππ« πππ₯π. Today at 6pm.
26/05/2026
Inu munadutsako mu nyengo imeneyiπππΎ
If this is your season right now...i wish you strength, Grace and healingππ½
Ngati mukukanika ndi kupemphela komwe chifukwa cha ululu, dziwani k*ti Mulungu amawona misonzi yanu ndipo amamva kulira kwanu. I've been here before. I know π«
We Gonna Heal.
Good Nightβ€οΈ
Click here to claim your Sponsored Listing.