Tinakumana Pano

Tinakumana Pano

Share

Communication education e t c���

03/06/2026

Taonesetsan msanayambe kuganiza

09/05/2026

Boss dzulo munatipasa cross koma mkaziyo anali chibwenzi Cha a friend athu panopa anasiyana of course namuuza kt atumize pic koma vuto wap wanga anandipanga bun kuti zikaona basi tinangolumikizana pama text.
Phone yangaso ndi ya new one number yake nalinayo mu phone ina yakale . Anafika pa yad wagogoda pa get ine chongosegula get mkazi nde anauma waithyola akuti akusaka nyumba ya rent !😂 Ndinamuuza kt mayazi mesa ndiwe amene timayankhulana pa phone uja and wandiuza zot uli pa get that why ndabwela kuzakusegulira akuti ai sine basi wayamba kubwelera nayesela kumuimisa koma sizinatheke. Madzulo tagona wandilembela message akuti wandituma ndi Ex wakeyo ndimuuze asiye kumalonda then wandipanga block kuyesa number ina wapangaso block

Nde mafuna mundithandize man muyankhule naye mumuuze ineyo ndili serious of course zachitika by mistake komabe ineyo ndamukonda osatiso za hit and run ai koma za serious tikhale pa chibwenz . Iyeyo chibwenzi ndi Afriend athuwo chinatha kalekale and Afriend wo pano anapita theba koma saziwa mkaziyu nde akuona ngt ndi plan ine ndi Afriend yo and I try kumufotokozela kt number yako ndatenge kwa mike koma sanavesa akt number nalinayo kale.
So Ndingofuna mukambe naye zikathela fanta mumwa Chonde bro mkaziyu nane ndikamufuna kalekale

09/05/2026

Hide my I'd ndine mulendo pamudzi pano timafuna cross mumatani😚 tipezeleni wot kucheza naye basi atigaile ndalama🤫 pepani ndangofikira pakati ine gal age 23 ndimakhala ku Lilongwe area 23 chaku thaki . If possible mamuna akhale wa around Lilongwe olo panopa titha kukumanatu 🫣😱 ndili paselipa mundiuza zikatheka Zikomo.

(area 23 ana abwino awa ana a sho sho no mistake)

09/05/2026

Palibe mamuna ofasa pakhani zogonana ngati wanuyo ngofasa amakakhala dolo kwinakwake good afternoon 😀

11/02/2026

🙆🙆🙆🙆🙆😂😂🙌

Telephone