Alkhuwet mw
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Alkhuwet mw, Health/Beauty, Bangwe, Blantyre.
28/09/2025
Asogoleri akumalawi
17/03/2025
Penapake nkumati malawi ndi dziko kapena matenda 🙈🌚
16/01/2025
ZINA UKAMVA.ðŸ˜ðŸ˜ðŸ˜
(ZOCHITIKA PA DZIKOLI)
Mudziko la Zambia mwatekeseka pamene apolisi amanga mayi wina yemwe ndi prophetess kumeneko dzina lake Sylvia Mutoba.Mnyumba mwa maiyu mwapezeka thupi lakufa la mwamuna wake yemwe wakhala akusowa kwa zaka ziwiri koma thupilo lapezeka lili mafupa okhaokha titagonekedwa pa bed mu chipinda china cha mnyumbamo.
Polengeza nkhaniyi pa Diamond Tv, mchimwene wa munthu omwalirayo wafotokoza kuti iwo monga a ku banja akhala akusakasaka m'bale wawo yemwe anangokhala ngati wasowa, koma mlamu wawo yemwe ndi mkazi wamalemuyo amakaniza anthu kufika ku nyumba yawo.
Opolisi popangabe kafukufuku ofufuza a George Kalaba, omwe anasowawo omwenso anali osewera mpira wakale wa timu ya Zanaco, apolisi anakwanitsa kupita ku nyumba ya mai wo komwe anapeza khomo lotseka koma anthu ali mkati, ndipo atalowa anali odabwa kupeza thupi lamunthu wakufa litasala mafupa okha pa bed m'chipinda china chomwe chipindacho chinali chotseka ndipo samalola anthu kulowako.
Apolisiwa akusunga muchitokosi mai Sylvia Kalaba, azaka 51, pamodzi ndi ana ake anayi omwe ndi Natasha, 19, Sandra, 22, Wendi, 27, komanso mwana wina wa zaka 15 ndipo kafukufuku ali mkati pofuna kuziwa zambiri pa nkhaniyi.Koma mai Sylvia Mutoba akana zoti anapha amuna awo.Iwo ati amuna awo anamwalira atadwala matenda a mphumu( asthma.Mai yu wati anasunga ma skeleton a mwamuna wake chifukwa amamuthandizira kupanga ma miracles pa utumiki wake wa u prophetess.Iyeyu akuti anauzidwa ndi msing'anga wina wa ku Tanzania kuti mwamuna wake akadzamwalira ,adzamusunge mnyumba mpaka adzavundire momwemo ndipo ma skeleton ake adzakhala ndi chikoma choitanitsa ndalama kuchoka kwa anthu kupita kwa mai yu yemwe ndi prophetess ndipo izi zakhaladi ati zikumuthandiza mai yu chifukwa kumpingo wake kumabwera chinamtindi cha anthu komanso amapha makwacha.
03/04/2022
Malawi ziko la mkaka nd uchi kma momwe zililimu zikugwilizana nd kukhala ndi mkaka nd uchi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Bangwe
Blantyre
MRTHETACER