Blessed Herbals
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Blessed Herbals, Health/Beauty, Blantyre.
19/04/2026
Ambiri mpoloni mukuwuziwa .mtengo uwu osapanga nao chibwana the most holie holiest three paziko pano . Vuto lina lililonse lomwe mulinalo osavutika kupita kwa asinganga ayi .
Kaya mufuna kuwina mulandu kapena malo omwe mwagula inu pakuchuluka zitopotopo kungopeza mtengo umeneu kuwuwuza zochota umanva this is the tree that connect you with God directly trust muli pachiphinjo muli pamavuto olo familly yanu ili pachipopsezo chachikulu mwakhala mukulonjezedwa zosiana siyana kaupezeni mtengo wa mpoloni you will get your answers instantly or through your dreams.mtengo okongola muntima uwu olo pachiopsezo chotani mtengo uwu ndichipha mtima olo njoka singakulumeni ataa
Nyumba mwanu mukuchitika zaufiti zosiaya siyana olo mwagula malo omwe pali makangano oti m***a kuluza moyo kaupezeni mtengo wampoloni.mfiti ndi mtengo uwuu nde kutali tali
Munali munthu oyipa mwapanga nyasi ne mtima wanu ukungosowa mtendere olo kufuna kuzimangilira kumene kaupezeni ntengo wampoloni
Kaya busness imene Kaya ndipa company mwakwezedwa udindo nde muli ndi Mantha kaupezen mtengo umeneu
It has so many spiritual aspects titha kuchezere panopa kufotokoza za mtengo wampoloni.God gave us everything we need through the power of nature koma anthu sitiziwa ayi.
Inuo kungosamba mpoloni nothing can shake your life zilipo zinthu zitatu zomwe timasakaniza when it comes to cleansing tibwera nao topic
Omwe muli ndi mtengo uwu your blessed ndipo osadula uchengeteni komanso ngat mwakumana ndi post iyi ndinu odala, omwe mungaufune Whatsapp 0888213553.
Zikomo!
30/03/2026
Munamvapo Zotani Zokhuza Black Seeds? nanga Red ♥️ Jatropha??
Zoti zimalimbana ndi kugonjesa matenda, tizilombo/mavayilasi mumaziwa???
Akuti kuli matenda opanda makhwala? Mmmmh inu ganizaniso kawiri, pano za Corona-Vayilasi mene inathera Boma linafotokoza ngati? Komatu amati Corona nayo yabwera kuzakhala ilibe makhwala, Komanso HIV ndi Corona or Ebola zoopya ndi zinazi...
So why HIV yokha ndi yomwe imangokambidwa Kwa nthawi yayitali... Koma Ili yosaopya ngati Corona or Ebola?
Boma limapeza ndalama, zithandizo kuchoka kunja mu dzina la HIV, anthu ena ochuluka analembedwa ntchito mu dzina la HIV ndiye kuti avomereze kuti imatha kutha samafuna dala...
Inuyo mumakhulupilila kuti MULUNGU ndi wa mphabvu ndipo palibe chomlaka, koma ikafika nkhani ya HIV ndiye munachivomereza kuti basi ndiyamyaya ilibe makhwala or singathe??
Munamvapo za ma herbs a BSM opangidwa ndi a Blessed Herbals ?
ma herbs awa mumasakanizidwa ma ingredients odusa 10, kuphatikiza Black Seeds, Red Jatropha, Cinnamon, Neem, Moringa etc...
Zomwe zili zampabvu pogonjesa matenda, kupha tizilombo, mavayilasi, ma bacteria 🦠 etc...
Komanso m***a kumwa ma herbs Amenewa or musakudwala pongofuna kungopanga service thupi, kusuka magazi, kuchengetera umoyo...
Imbani 0888213553 or Whatsapp kuti muve zambiri, mupeze nawo or muwapezere achibale or azanu ma herbs Amenewa...
Zikomo!
03/02/2026
💊💊🦠ZOTSATILA ZOGWILITSA 💊NTCHITO MA ARVS💊🦠 KWA NTHAWI YAITALI 🦠💊💊🦠💊
🦠Pamwamba pa kutalikitsa moyo ndikuchepetsa chiopsezo chopatsila anthu ena matenda a HIV, palibeso ubwino wina umene umanene kuposela kuipa kwake, tiyeni tikhalire limodzi.
🦠💊Amapangitsa kagawikidwe ka mafuta mthupi kukhala kosiyana(Lipodystrophy syndrome)
🦠💊Amapangitsa kuti mafuta achoke mmiyendo ndi mmanja(Lipoatrophy)
🦠💊Amapangitsa kuti mafuta amene achoka kumiyendo ndi mmanja adzazane pa mimba, mmusi mwa khosi, mmikono ndimu ntchafu(Lipohypertrophy)
🦠💊Amabweletsa mavuto a mafupa(osteoporosis)
🦠💊Amapangitsa abambo kukula mabele(Gynecostia)
🦠💊Amasokoneza ubongo kupangitsa munthu kumakhala Ngati mutu wake sugwila bwino
🦠💊Amayambitsaso stroke pamene awononga Spinal cord ndi ubongo
🦠💊Amabweletsa mavuto oiwalaiwala
🦠💊Amasinthitsa kakhalidwe, ma mood swigs osaneneka
🦠💊Amathandizila odwala kumakhala ndi nkhawa komaso opanikizika malingaliro.
🦠💊Amapangidwa odwala kukhala munthu osakhazikika pa zimene akupanga
🦠💊Amabweletsa matenda a sugar, kusaugwila bwino kwa liver komaso ma kidneys
🦠💊Amabweletsa vuto lokanika kugona
🦠💊Amathandizila odwala kukhala mmoyo ozisankha, ozipatula ndi osasangalala mmagulu amzake.
🦠💊Amaononga mitsempha zimene zimapangitsa kumava kutentha miyendo ndi mapazi ngakhaleso dzazi losatha.
🦠💊Amadetsa nkhungu Maka muzikope za diso komaso mmusi mwa diso
🦠💊Amabweletsaso vuto la kusokonekela kwama hormones zimene zimathaso kukhudza ubeleki wa Mai komaso zotupa za kumazila, mkati ndi kunja kwa chibelekero.
🦠💊Amasinthitsa kaonekedwe ka thupi, khope imaphwangika, miyendo imaphwanyika, manja amaphwanyika koma mimba, khosi ndi mapewa zimananala.
NB: Si aliyese amene akugwilitsa ntchito ma arvs angaone mavuto awa, amasiyana thupi ndi thupi ndipo wina akhoza kukhala mavuto ochepa kuyelekeza ndi wina.
🧬Kupanga masewelo olimbitsa thupi, kumadya zakudya zamagulu onse, komaso uphungu ndi upangila wakakhalidwe ndizina zomwe zimathandizilakobe kuti mavuto awa asabwele kwa amene akhudzika ndi mavutowa.
🥦 Pogwilitsa ntchito mankhwala opangidwa kuchokela ku chilengedwe amene amakhala ndi zowayeneleza zothanilana ndi mafuta amene aundikana Malo amodzi, mitsempha yaonongeka, ziwalo sizikugwila bwino ntchito ndi kuthana ndi mavuto ena onse amene abwela chifukwa Cha mavutowa ndizo njira zomwe zimagwilitsidwa ntchito pothanilana ndi mavutowa.
Nkhani yabwino ndi yokuti ife a Blessed Herbals tili ndi ma herbs othana ndi ma virus, kuchosa maside effects a ma ARVs... 0888213553
20/10/2025
🍅 Tomato mukuwonayu ali ndi poison owopysa kwambiri.
Za white zomwe zamelazo ndi fungus (Aspergillus flavus ndi A. parasiticus). Ndipo dziwani kuti fungus ameneyu amatulutsa poison owopysa otchedwa aflatoxin. Aflatoxin ameneyu amawononga thupi pang'ono pang'ono. Pakupita kwa nthawi, amawononga chiwindi ndi kuyambitsa khansa ya chiwindi.
Zilibe ntchito kuti kaya mudula powolapo nkutaya, kaya mutsuka, kaya mumubwatitsa kwambiri, fungus yo samafa ndipo samachokamo.
Blessed Herbals - 0995 50 63 76
23/09/2025
Congratulations 🎉 DPP and APM
Mu nyengo ino ya zisankho ife a Blessed Herbals tasisa ntengo wa ma herbs anthu a BP, Diabetes, HIV ndi akuchipinda...
Inu a ndale, musafe ndi ma BP, Komanso kulephera kugwila ntchito kuchipinda chifukwa cha kukukhumudwa, or overexcited ife tilipo...
Pali ma herbs ena m***a kumwa ngakhale musakudwala kungopanga service thupi kusuka magazi, kuchengetera umoyo...
Imbani or Whatsapp 0888213553
Zikomo!
07/09/2025
Taluza miyoyo ya anthu awiri ogwila ntchito zachipatala mosayembekezera in less than masabata awiri chifukwa cha nthenda ya Asthma. MTSRIP.
Tiyeni tisamaphwekese ma herbs 🌿☘️ achilengedwe, mukuziwa kuti Asthma Ili ndi makhwala amphabvu otchedwa Asthma W**d?
Zomera zokuti zimangozimerera zokha manyumba mwathumu, koma ambiri timazipepusa, mumafuna makhwala achizungu, Indian, or Chinese okha...
Ife a Blessed Herbals timapanga, kuphuzisa, kulimbikisa za makhwala achilengedwe achi Malawi... Timapanga makhwala ngakhale othana ndi tizilombo ta ntunda wa ma vayilasi, kupheratu, kukweza chitetezo, kuchilisilatu, Zakuchipinda.
Palinso ma herbs ena omwe timalimbikisa anthu kumwa ngakhale musakudwala kungopanga service thupi kusuka magazi, Kupangisa thupi likhale mchimake, liziyenda bwino.
When last did you service your body? Mukudikila muzadwalekaye?
Anthu akuyitanisa ma herbs athu ku Australia, America, UK, RSA inu muli Mmalawi momuno?.
0995 50 63 76.
07/08/2025
🦠KWA OKHAWO AMENE🦠 ANAPEZEKA NDI MATENDA A HIV 🧬and AIDS🧬🧬
🦠KODI MULI NDI ENA MWA MAFUSO AWA?! 🦠
🦠Kodi ndizakhala chonchi mpaka liti?
🦠Kodi nditasiya kumwa mankhwalawa chingachitike ndi chani ku moyo wanga?
🦠Ndizinthu ziti zimene zingandithandize kuti ndizikhaka ndi moyo wathanzi ngakhale ndili ndi vutoli?
🦠Ndi zinthu ziti zimene sindikuyenela kuchita nawo, kudya nawo zomwe anthu amene alibe vutoli amapanga?
🦠Ndingatani kuti ndisapatsile anthu amene andizungulira komaso okondedwa anga?
🦠Kodi nditafuna kubeleka, sindingapatsile mwana wanga vutoli?
🦠Kodi ndi zotsatila zabwino ndi zoipa ziti zimene ndingayembekezele chifukwa Cha mankhwala ndikumwawa?
🦠Kodi Ndingatani kuti ndi ndithane nalo vuto limeneli pa moyo wanga?
🦠Kodi ndikuyenela kuti ndizikhala odandaula ndi osasangalala nthawi zonse chifukwa Cha vuto langali?
🦠Nditani naye munthu uja anandipatsa matendawa? Ndidane naye kapena ndivomeleze kuti nayeso sikunali kufuna kutengela?
🦠Kodi mchifukwa chiyani anthu amene anabadwa Ali positive akhala akumwa mankhwala kwanthawi Yaitali sasinthika thupi maonekedwe, nkhope, mikoni ndi miyendo or mimba pamene anthu amene tapezeka nayo titakula kale nkhope zathu, mimba zathu, miyendo yathu, kaonekedwe Kathu kakusinthika chonchi?
🦠Kodi popeza ndili kutali ndipo mankhwala sindikumwa, ondilandilira or ondibweletsela palibe, Ndingatani kuti ndikhalebe ndi moyo wanthazi ndi wamphavu?
NGATI MMAKHALUPILIRA KUTI MULUNGU AMACHIZA NDIPO ANGATHE KUTHANA NDI VUTO LANU, NDIPO PALIBE NTHANDA YOSACHIZIKIZA, MUNAVAPOSO KUTI ENA ANAKHALA BWINO ATAKHALA NDI VUTO NGATI LANULO, NANUSO NDIZOTHEKA.
Simukuyenela kumadandaula ndi vuto lanu kwambiri chifukwa mmene ikuzuzila anthu BP ndi Sugar, mukanakhala pansi ndikuyamika kuti Ambuye mwandikondela, sindikuyenela kumadandaulaso.
Ngati muli ndi mafuso awo ndipo mulinacho chidwi chodziwa ndikuphuzila zambiri ngakhaleso kupeza nthandizo kumene Tilankhulane
WHATSAPP 0995506376
07/08/2025
🫄🏻🫄🏻🫄🏻KUCHOTSA MIMBA🫄🏻🫄🏻🫄🏻
🫄🏻Posatengela kuti dziko kapena chipembedzo chimati chani pa nkhani yochotsa mimba,ndi udindo komaso chisankho amene ali ndi mimbayo kukhala nayo kapena kuchotsa,koma chisankho chili chonse chili ndi zotatira zake tiyeni tione.
UBWINO OCHOTSA MIMBA
🫄🏻Umakwanitsa kumaliza school ngati watenga mimba uli pa school
🫄🏻Umaonekabe mtsikana pamaso pa amzako
🫄🏻Umapitilira kulandila chikondi kwa makolo or achibale popeza sadziwa kuti wachotsa mimba
🫄🏻Umapitilira kukondedwa ndi abwezi ako ngati mtsikana
🫄🏻Umakhala wachotsa nkhawa yoti uli ndi mimba
🫄🏻Umakhala wazionjezela nthawi yokhalabe mtsikana.
Ma ubwino amenewa ndi ena, ndamene anthu ambiri amaonela kuchotsa mimba ngati njira yabwino yokwanilitsila zomwe akufuna, koma posatengela kuti muli ndi zolinga zanji, mavuto awa azakulondolani pafupike patali chifukwa cha chisankho chochotsa mimba munapanga,
1. Kukanika kutengaso mimba
2. Period yosalongosoka
3. Kutha kwa chilakolako chogonana ndi mamuna or atakugwilani bwanji
4. Kutenga mimba kumangochoka
5. Kubadwitsa ana akufa kale
6. Zotupa za mchibelekelo
7. Zotupa zaku mazira
8. Zotupa za kunja kwa chibelekelo
9. Kutsekeka kwa ma tube
10. Kudyeka kwa cervix komaso chibelekelo
Mavuto awa ndiwo amabwela chifukwa cha chisankho chomwe munapanga chochotsa mimba, tsono izi zimadza mutamaliza BWino bwino kaya maphuziro anu, sinanga munaona kuti mimbayo ndichipsinjo ku school yanu, pa nthawi iyi mmakhala muli pa ntchito yabwino, banja labwino zonse zikukuyendelani, koma pamene mwaona kuti mavutowa adza, mumakhala mukupanga regret pozindikila pamene panachoka vuto lanu.
Mmayesetsa kuzibisa ngati vuto si inu, kuloza zala amuna anu, kuloza zala abale kuti ndiwo akulodzani chosecho mukudziwa gwelo lake.
Akazi onse amene anachotsa mimba masiku awo akunjoya komaso school, mavutowa akadza, ndamene amakhala patsogolo kupakizila ena vuto lawo, komaso sizitheka kumuuza mamuna wawo osalakwayo kuti inetu izi zikubwela chifukwa mnachotsa mimba ya X wanga before you.
Ndimati mkudandaulileni, kaya mavutowa abwela kale pa moyo kaya sanabwele dziwani kuti simungasinthe kale lanu, kukhala mma regret sikungakuthandizeni kalikose, Chifukwa mkuvomeleza ndikupempha chikhululuko kws Mwini Moyo Mulengi Chiuta Namalenga, kenaka ndikuyamba kusaka thandizo loyenela kuti vutoli lithe ndipo ngati kusabeleka kukuvuta koma chibelekelo chilipo m***andizikeso.
Ngati simungakwanitse ndithu kumasukila amuna anu gwelo la vuto lanu poteteza banja lanu kuti akadziwa ingalakwe, tili pano kuthandiza anthu ngati inu, bola kunena chilungamo kaya mwakhala mukuchotsa mimba maulendo angapo kaya kamodzi komaso njira zomwe munagwilitsa ntchito, mwa izi perhaps Inshallah Mungathandizike.
WhatsApp/Call 0995506376
Shalom.......
07/08/2025
🥐🥐🥐KODI MUKUDZIWA KUTI MATENDA A 🥐SICKLE CELL🥐 NDI OTHEKA KUCHIZIKILATU?🥐🥐🥐
🥐Matenda a sickle cell ameneso amatchedwa kuti sickle cell disease (SCD) ndi nthenda imene imakhudza ma genes ndipo imakhudza hemoglobin yomwe ndi protein imene imakhala mmagazi mma red blood cells yomwe imanyamula mpweya kupitsa magawo osiyanasiyana a thupi.
🥐Chomwe chimachitika kuti munthu akhale ndi vutoli ndichakuti, munthu amakhala kuti anatengela Ma abnormal copies awili a hemoglobin gene (HBB) imodzi kuchokela kwa Bambo imodziso kuchokela kwa Mai.
🥐HBB gene ndi imene imalamula kachulukanidwe or kapangidwe ka hemoglobin, ndiye chifukwa cha mutation yochitika mu HBB gene 🧬, hemoglobin amene amakhala akupangidwa amakhala wa abnormal, ma molecules ake amakhala atalitali kupanga mwa chain, izi ndizimene zimapangitsa kuti Red blood cell yomwe iwo aliyo ipindike komaso ikhale yolimba mkumaoneka ngati zenga( sickle).
🥐 Pamene ma abnormal hemoglobin cells amenewa akupangidwa, chiwelengelo chawo mthupi chimakhala chikukwela, popeza amakhala opindika ngati zenga/chikwakwa, mayendedwe awo mmitsempha amakhala ovuta kwambiri, mwakuti amatha kutsakamila mkutseka mtsempha magazi mkusiya kumadutsako zomweso zimatha kuyambitsa matenda a stroke.
🥐 Chifukwa cha kuchuluka kwa ma abnormal cells amenewa, popeza mumakhala ndithu hemoglobin, amakwanitsa nthu kunyamula mpweya monga ma normal red blood cells amachitila, koma vuto limakhala lakuti, mpweya umenewu umakanika kuti utsitsidwe ku ma cells komwe afikako pamene ma normal red blood cells amatsitsa mosavuta kuti ma cells azigwilitsa ntchito mpweya umenewu, chifukwa chakuti ma abnormal cells amenewa samakhalitsa amafa msanga, izi ndizimene zimapangitsa kuti munthu ayambe kukhala ndi vuto lothaitha magazi komaso azikhala ofooka kwambiri ndi mutu uzimuwawa kwambiri.
Odwala nthendai,amakhala ofooka,amatha kumatupa nkhope manja,mimba or miyendo,magazi amatha pafupipafupi,amachedwa kukula maka ana,amakhala ndi thupi lonyozoloka losasangalala
🥐 Chomwe chimayambitsa matendawa monga ndifotokoza kale ndikutengela ku mtundu ndiye gwelo lalikulu,komaso zinthu zina monga kuchepa kwa madzi mthupi,kuzizila kwa nyengo,kukhala malo okwela (high altitudes areas),kupanikizila mmalingaliro komaso ma infections amathaso kupangitsa kuti vutoli liyambe.
🥐 Chifukwa cha vutoli,ziwalo zikulu zikulu ndi zofunika kwambiri zedi za mthupi ndizimene zimakhudzika kwambiri monga, impsyo,mtima,mapapo,chiwindi ndi ubongo.
KODI SICKLE CELL DISEASE NDIYOCHIZIKA??
🥐Pali njira imodzi yokha yomwe chipatala chimagwilitsa ntchito pochiza vutoli,koma zipatala zakwathu kuno Ndizovuta kwambiri, process yake ndiyaitali mwakuti ambiri odwala mavutowa akuti afunika alandile thandizo lothetselatu vutoli amayenela kutumizidwa zipatala zakunja zapamwamba kwambiri.
Njira imene imagwilitsidwa ntchito ndi ya BONE MARROW TRANSPLANT yomweso imatchedwa kuti STEM CELL TRANSPLANT.
Mu njira imeneyi,choyamba ma dokotala amapeza m'bale wa odwalo ndikumuuza ngati afanane magazi,akafanana,amatenga odwala uja ndikumuipa pa treatment ya chemotherapy kapena radial therapy kuti aphe bone marrow ya odwalayo popeza ndimomwe ma red blood cells amapangidwilamo,zikatero amatengaso m'bale uja (donor), ndikumung'amba bone marrow yake munjira ya surgery ndipo amatengamo bone marrow yake ndikuika mwa odwala uja mmagazi direct,zikatele bone marrow wa m'bale uja ayamba kupanga ma red blood cells abwino bwino mthupi zikatero ndiye kuti sickle cell anemia/disease imakhala yathela pomwepa kOma ngozi imakhala yakuti,bone marrow wa m'bale uja akakhala kuti wakanidwa ndi thupi la odwala uja ifa imachitika pasanathe 24hrs.
🥦NKHANI YABWINO NDIYAKUTI🥦,
Njira yoononga kaye bone marrow wa odwala kuti thupi lake lisapangeso ma red blood cells a abnormal ndiyoipa kwambiri popeza imakhalabe ikuika chiopsezo chachikulu kwa odwalayo,pali mankhwala achilengedwe amene Ali ndikuthekela kwakupha bone marrow mwa amene ali ndi vutoli nthawi yomweyo bone marrow yatsopano nkumapangidwaso popanga surgery iliyose or infusion iliyose.
Mankhwala amenewa ali ndi immunosuppressive komaso cytotoxic effect ku bone marrow.
Ena amati ndimabisa mankhwala koma lero mudziwa,mankhwala ake ndi awa
🥦Arsenicum album amene amapha bone marrow
🥦 Podophyllum amene amakhala ndi podophyllotoxin emwe amakhala ndi immunosuppressive effect
🥦Taxus spp yemweso amapha ma bone marrow
🥦 Cyclophosphamide-Containg plants eg cycas revoluta ameneso timagwilitsa ntchito pothana ndi cancer amakhala ndi cyclophosphamide yemwe ndi 50:50 ndi chemotherapy.
Mwachidule,ndi njira zachilengedwe sickle cell anemia or disease imatha mma stage atatu omwe ndi
1. Toxicity
2. Immunosuppression
3. Cytotoxicity
Note: Njira ya chilengedwe yogwilitsa ntchito mankhwala amenewa opha bone marrow ndikupanga wina watsopano wakuti azipanga ma red blood cells abwino bwino,ndi njira yomwe siyachibwana ndi imene ndiyofunika kugwilitsa ntchito ndi kapena kupelekedwa ndi okhawo omwe amazitsata izi osangoti chisawawa ma herbal mkumati sickle cell itha ai, herbal medicine specialists only.
Odwala ayenelaso kulandila uphungu wa zakudya zoyenela ndi zosayenela komaso ayenela azimwa madzi okwanila pamene ali pa dose imeneyi shalom.......
Mafuso aliwose ndi olandilidwa fusani p***a kapena sindikizani WhatsApp button ili mmusiyi
WhatsApp/Call 0995506376
06/04/2025
Kolona Vayilasi inatha, Ebolaa Vayilasi inatha, HIV siyoopya kuposa ma Vayilasi enawo koma ndichifukwa Chani HIV amayipopa kwambiri or safuna kuvomereza kuti imatha mpaka dzaka zambiri kumatha??
BOMA, Mabungwe amapeza ndalama/zithandizo zochuluka mu dzina la HIV ndiye kuti avomereze kuti HIV imatha samafuna coz anthu ena ntchito zizawathera, Mabungwe ena azasekedwa, ndalama ndi zithandizo zizasiya kuperekedwa...
HIV inayamba dzaka zoti Dziko lapansi idali isanatukuke ndiye information imabvuta kugawana, pomwe matsiku ano kolona Vayilasi inabuka anthu amagawana ma remedies mophweka kuzera ma social media, zomwe kale kunalibe ndipo zinathandizila kuti kolona igonjesedwe mosabvuta...
Koma Moopa Mulungu tikukusimikizilani kuti zikumatheka ndithu tizilombo ta HIV kutheratu kubwerera negative ndithu ndi Blessed Herbals Mixtures.
Funani ndipo muzapexa, gogodani ndipo muzasegulidwa, palibe bvuto lopanda yakho 0888213553...
30/03/2025
Kodi mumaziwa kuti dziko la Sasafrika 🇿🇦 ku Johannesburg ndi komwe HIV iliko kwambiri??
Ma report akuti Kwa nthawi yoyambaakatswili ena kumeneko apanga makhwala ochiza HIV inde kuthanilanatu ndi tizilombo tosausa tamavayilasi timeneti.
Koma ife a Blessed Herbals tinaziwa kale kale za makhwala othana ndi HIV, ndipo titha kukusimikizilani kuti ma herbs athu amayenda/kukondedwa kwambiri ku South Africa.
Kumbukilani kuti makhwala ena amagwila bwino ntchito malinga ndi Environment, or mtundu wa munthu nanga Munthu wachimalawi, Wachi Africa kumamwa Chinese herbs zingagwile bwino ntchito?? Yes some times but not efficiently...
Therefore enafe mayakho anthu ali mu makhwala omwewa onyozeka achi Malawi achi Africa, omwe amapangidwila ndi madzi okokuno osati madzi achere amayiko enawa...
Whatsapp 0888213553 kuti muve Zambiri pa Whatsapp.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre