MR 3 B

MR 3 B

Share

LOVE CONNECTOR AND OTHER GOOD STORIES wapp me on +265888545597

30/08/2026

Ntsikana wazaka 20 pa Namitete ku Mchinji amakhala ndimakolo ake

Akufuna mwamuna wamkulu oti azimvana naye and azimuthandiza or kumupangira rent azikhala yekha k*ti mwamunayo azitha kumuyendera mosavuta

Kantsikanatu kowala

Ñdipezeni azibambo pa 0888545597

30/08/2026

Munthu akulipirireni ya rent mukhala mnzake ???

Ndatitu mnzake zinazo zizikaoneka konko

30/08/2026

Noma vs Ekhaya itha bwanji

Bundle ya week yamunthu wamphumi

30/08/2026

Mwaswera bwanji uncle, munithokozereko kwa phiri Gift anithandiza ni 3200 ya kamba wa birthday ya miracle nik*ti zikomo kwambiri ambuye akudaliseni 🙏

30/08/2026

Hie admin post Ku guluko ndikugulisa gotv ndakhala nayo 6 months only

Ndikufuna ndipeze ya rent zandivuta mtengo wongondithandiza 35K ndiri Ku Blantyre mbayan

# sindikapo Ena amangotenga aziyankhula zopepera kupewa Izi ndisatira macoment

30/08/2026

Nsithokozereni kwa Mr Falanga andithandiza ndi ndarama yokwana 5500 ambuye apitilize kuwadalisa, zikomo kwambiri.

lne Tira

30/08/2026

Mr zikomo kupost inja mmati tipemphe zammawa ine mnalemba k*ti winaangondigaira 1700 ya 1kg yaufa koma ndamuona mulungu ndithu brother Noah Matengo andidalisa ndindalama yokwana 3500 mulungu awadalise ndithu ana anga adya masana uno ndithu

lne Ririan

30/08/2026

Hello brother,munaponya post yoti titumize p*k ndipo munati itamuwaze atumize 5000 pin,ineyo ndimodzi yemwe ndinaponya nawo ndipo ndazizimusidwa ndi 2pin ,ambuye awadalitse sister ena ake pa group pano andigaira ndipo ambuye awadalitse ndikuonjezera pomwe achosapo.ine felister.

30/08/2026

Mwadzuka bwanji Mr 3b mundithokozele kwa Noah pa post yok*t tiponye pic mwina wina nk*tithandiza ndi 5pin ine naponya nkulemba k*t olo 2pin njambili ndye aunvle Noah analowa inbox nkunena k*t ndapase number ya airtelmoney andiponyele anditumizila 4pin ambuye awadalitse

lne Beauty

30/08/2026

Mr 3 b ine kuno kwanga ndikunthokoza ku through forum ino ndaziwana ndi azichimwene komanso ma ccta achikondi and amandimvesa kukoma kwambir 😭😭😭😭 misozi Yanga ndi ya chimweme kwambir chifukwa cha anthu amenewa sindwatchula Koma aliyense amve Kuti ine ndimawanyadira and mulungu aziwafewesera nyengo zawo nthawi zonse nane tsiku Lina ndikudziwa mulungu azatsegula makomo anga Kuti ndizanthandizenso ena to you Mr 3 b inuyo ndi mulelankhungwa mulungu azik*tsogolerani happy Sunday to u all ine Shira chinkono

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


BLANTYRE
Blantyre