HANET mw kukometsa
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from HANET mw kukometsa, Health/Beauty, Chiladzulo, Blantyre.
27/07/2023
Mwana wanga oyamba nde muziti osokhelana mulandila ma pama
THE GAME OF LOVE part 1
Ine ndi Ganet yemwe ndili ndi anzanga awili ben Kay kmanso mphatso tonsefe ndisaname tachedza bwino
Kuyambila kale takhala tikupaga zithu mwa mpikisano ndipo ndi moyo omwe timava nawo bwino mpikisano wathu amachitika my dzithu idzi
Zovala,ndalama,school kmanso akadzi
Zimenezo ndizithu zomwe timapanga kma panopa ndinasiy chifukwa ndine muthu ochita bwino kwambili ndipo pa zithu zomwe timapangazija chithu chimodzi ndi chomwe chinandifikisa pano
Chikondi khani yanaga yachikondi inali motele
Sikulina tikupita ku school 🚸 kunali ka vula ndithu ndipo linali siku lo bowa mix kudzizila tikuyenda pandusa galimoto ndipo linatithiala matope
Kma muthuyo sanaime ndipo galimoto inalunjika ku school kwathu ife tinayenda mpaka mkalasi
Mwini galimotoyo anali mphudzisi wa nyuwani yemwe amadzasiya ma file ake a transfer sipanatenge thawi kunatulukila galimoto lomwe linanyamula katindu wa mphudzisiyo ndipo zinali motele
: okay kwabwera aphudzisi asopano nde tikawathandize kunyamula katundu
: yeah yeah ✌
Ndipo tanapita zonse zinayenda bwino
Mawa kutacha ndinapita ku school mochedwa nditalowa class ndinaona mwana kuwala mwana nyenyezi utawaleza omwe sinaonepo
Ndipo ndinali odabwa naye nditafika
: Ganet ukuchoka kuti thawi zino
: kunyumba sir
: Kodi umakonda kuchedwa chifukwa chani
: sir mayanga achokapo nde ndimagwila mchito za pakhomo
: mmmmmmmm
Amatelo chifukwa amadziwa kuti ndikunama
: mwana wabodza iwe takakhaleni musanditayise yesu
Ndinakakhala ku back ndi anzanga ben kay kmanso mphatso ndipo zinali motele
: madolo mwaona zomwe ndaona
: ndi zina zomwe sunaone
: kma akaka nde ndigwila
: okay
: sangakulole ulibe kalikonse iwe
: tiona
Class inavuta ndipo kunali mpikisano nkaziyu anali nwana wa aphudzisi omwe anangofika kumene aja
Nthawi ya break itakwana anyamata kunali kukambalana kma poti aliyense amafuna ndipo panalibe ogonja zinalowa mu game
Wait 2
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Chiladzulo
Blantyre