HerbBank Mw
The home of organic herbs/food supplements(international standards) Lilongwe & Limbe
We provide free natural healing guidelines and sell herbs and food supplements
27/11/2025
KUTI MUBEREKE
PAKUFUNIKA MAYI NDI MZIBAMBO AKHALE NDI CHONDE NGATI PALIBE CHONDE TENGANI MA HERBS OPATSA MPHAVU NDI CHONDE FERTILITY mumafuna thandizo tipezeni Lilongwe ndi Limbe or call 0994726617
20/05/2025
LILONGWE SHOP; GATE LOLOWERA MA BUS AKULU (LILONGWE BUS DEPOT) OSALOWA KWEZEKANI PANG'ONO KU LEFT SHOP # 44
LIMBE PACIFIC TOWER SHOP /2.
Tili ndi ma herbs othana ndi mabvuto ambiri 1.body boost(hips/butts),
2.weight gain(male& female)
3.slimming/flat tummy
4.skin and toothcare
5.detox and immune booster
6.libido, fertility,sexual energy& other health problems
Helpline: 0994726617/0881495971
07/04/2025
*TUMERIC NATURAL SOAP*
Uyu ndi soap yemwe main ingredient yake ndi TUMERIC ndipo amathandiza izi;
1. ziphuphu(Pimples)
2. acne
3. Kuchotsa ma dark spots
4. Kuthana ndiziwawu zazuwa/mafuta
5. Kufewesa khungu
6. Kuwalisa khungu
7. Kuchotsa litsiro lapakhungu
Alipo lilongwe and Limbe at k7000 bar
07/04/2025
*C-4 Mankhwala ONENEPETSA THUPI opangidwa kuchokera ku zipatso*
Bambo, mayi mukufuna kunenepa? Kapena mwana wanu mukufuna anenepe kuonjezera minyewa koman kg?
Tili ndi mankhwala opangidwa kuchokera ku zipatso a *C-4 pills*
*Ubwino wa C-4 pills*
ali ndi ubwino uwu;👇
✓Kunenpetsa thupi momwe munthu ukufunira.
✓Amathandiza ana onyentchere kunenepa komanso kukula
Mankhwala a C-4 amagwiritsidwa ntchito ndi winaaliyense *Bambo, Mayi* komanso *ana*
Ndipo carton ya 100 pills timagulitsa pa mtengo wa k20,000. Imeneyo ndi full dose ukagula wagula basi wathananazo.
Mankhwalawa amathandiza ndi odalirika đź’Ż ndipo zotsatila zake zimayamba pakatha 7 days or 14 days.
*Mphavu za mankhwalawa zagona apa*
âś“ Amadzutsa mahormones opangitsa munthu kuti azikula kugwira ntchito yawo moyenera
✓Kuthandiza kuti munthu azidya moyenera ✓Kuthandiza munthu kuti azitha kugona tulo labwino.
Izi zimapangitsa munthu azikula komanso azinenepa kuonjezera ma kgz komanso minyewa.
Tikupedzeka ku lilongwe opposite kafoteka filling station kumanzere kwa nkhomo la bus depot shop number 44 Herbbank
Chiziwitso kwama customer athu.
Wina mwa katundu wathu wakwera ndipo mitengo yasopano ili motere:
✓Talatin from 14000 to k15000
✓C4 from k18000 to k20000
✓Chebe from k12000 to k15000
âś“ Tumeric soap still at K7000
✓warts remover still at K12000
✓All herbal tea's Still at K25000
Note: ma products ena onse alimwakale
Zikomo
04/01/2025
All available in our lilongwe and limbe shops.
✓Lilongwe we are located opposite kafoteka filling station kumanzere kwa nkhomoa lilongwe bus depot shop #44
✓Limbe we are in Pacific tower building shop number FFC10/2
Help line 0881495971
15/11/2024
*TURMERIC SOAP*
K7000 only
Amathana ndi;
1. Ziphuphu(Pimples)
2. Acne(ziphuphu zamabala)
3. Ziwengo
3. Zipsera
4. Makwinya
5. Chikanga
6. Kusalalisa mkuwalisa khungu
7. Skin allergy treatment
8. Kufewesa khungu
9. kuyeresa pokuda(dark knuckles)
LILONGWE shop and Limbe shop Kuli konseko timatumiza
Helpline 0994726617/0881495971
15/11/2024
*ANT-RHEUMATISM TEA*
K20,000 only
Uyu ndi Chinese herbal tea yemwe amathandiza mavuto monga;
1. nyamakazi
2. Zanzi komanso kuwotcha kwamapazi
3. Kuwuma kwaziwalo(minor stroke)
4. Kuwawa kwamma joint
5. Kubwezeresa cartilage mma joint
Kupatula tachulazi tea uyu amatetezanso munthu kumatenda a *mtima,cancer,Diabetes komanso kuchepesa cholesterol level wambiri nthupi.*
Akupezeka Kutali timatumizanso
Helpline 0881495971/0994726617
15/11/2024
*GE***AL WART CREAM*
K12,000 only
1. Ge***al warts (njerewere zakumaliseche )
2. Skin warts
3. Skin tags
4. Syringgoma
5. Kulogo
6. Corns
7. Skin mole
Effective in 7-14 days of usage only
15/11/2024
*WART REMOVER OINTMENT*
K12000
It removes;
1. ge***al wart
2. Moles
3. Skin tags
4. Acne marks
5. Scar
6. Flat warts
7. Foot pads
8. Common warts
Alipo
Call/whatsapp 0881495971/0994726617
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Limbe
Blantyre
Opening Hours
| Monday | 09:00 - 17:00 |
| Tuesday | 09:00 - 17:00 |
| Wednesday | 09:00 - 17:00 |
| Thursday | 09:00 - 17:00 |
| Friday | 09:00 - 17:00 |
| Saturday | 09:00 - 17:00 |
| Sunday | 09:00 - 12:00 |