Stylez Executive Barbershop

Stylez Executive Barbershop

Share

A world class executive barbershop offering professional hair styling, cutting and grooming services

12/06/2026

Machine mmanja, tiwale weekend imeneyi, only with StyleZ

Photos from Stylez Executive Barbershop 's post 07/06/2026

As we wind up the weekend, tili mtika....kuionesa!

Photos from Stylez Executive Barbershop 's post 05/06/2026

The weekend is upon us, tayambapo kale πŸ”₯πŸ’―πŸ’ͺ

Photos from Stylez Executive Barbershop 's post 04/06/2026

ZaleroπŸ«ΆπŸ’―πŸ”₯

Photos from Stylez Executive Barbershop 's post 01/06/2026

Pamene tikusangalala k*ti lero takwanisa 2years, ndiye tikungophulisa ma cut a clean okhaokha! πŸ”₯πŸ’―

Photos from Stylez Executive Barbershop 's post 29/05/2026

Ntchito za manja athu

fb.me 24/05/2026

Lero tithokoze ma customer anthu nonse posankha Stylez Executive Barbershop nthawi zonse...timakunyadilani

Monga mukuziwa kale, tili ndi ma barber odziwa bwino ntchito atatu zomwe zimapangisa k*t tik*thandizeni mwa changu

Malo athu ndi okonzedwa mwa pamwamba komanso aukhondo nthawi zonse pofuna kuk*tetezani inu komanso kukuchosani nkhawa pamene tikuk*thandizani

Tili ndi zipangizo zapamwamba za original ndi makono zometela mmutu, ndevu, mphuno, mmak*tu kuphatikiza apo tilinso ndi ma generator, gyser, CCTV, mipando yamakono zomwe zimathandizila k*t tizitha kuk*thandizani bwino ngakhale magetsi atazima.

Pitilizani kusankha Stylez Executive Barbershop nthawi zonse. Tipitiliza kugwila ntchito yabwino. Timasegula shop tsiku lirilinse from 8am mpaka 7 pm kupatula Sunday lomwe timasegula 10am. Tikupezeka konkuja Ku soche east shopping mall, near Sana shop, at kudya in Blantyre

fb.me

Photos from Stylez Executive Barbershop 's post 16/05/2026

Si mmene kulili...additional waiting area wearing a new face πŸ’―πŸ”₯πŸ‘€πŸ’­

14/02/2026

Feel confident on this Valentine's Day. Let us style you πŸ’ƒπŸ»πŸ•ΊπŸ’…

03/02/2026

Birthday wishes to our supervisor and front office assistant, Immaculate!!

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Soche East Shopping Mall (kudya)
Blantyre

Opening Hours

Monday 09:00 - 18:00
Tuesday 09:00 - 18:00
Wednesday 09:00 - 18:00
Thursday 09:00 - 18:00
Friday 09:00 - 18:00
Saturday 09:00 - 18:00
Sunday 09:00 - 18:00