Symon wazisomo

Symon wazisomo

Share

Advertising your business in this page with affordable price

20/01/2023

Nonse amene munatengedwa kuti ndiinu opanda pake Yehova akukumbukileni ,Chisomo chikugwereni kuti awo ozitcha okha amzeru ndi achumawo ukulu wa Mulungu auonere painuπŸ™πŸ™

17/01/2023

Mudzina la Yehova Mulungu wamakamu,afiti onse lero akhale pa tchuti ,asafike pakhomo panu ndipo ndiinu otetedzedwa.πŸ™πŸ™

17/01/2023

Ngati wakudzutsani ndi moyo lero akupatsaninso zosowa zanu lero.Ameneyo ndiye Yehova Mulungu wamakamu.πŸ™πŸ™

15/01/2023

Zilibe kanthu kuti zikuoneka ngati nyengo zanu zaipiratu.Koma musafooke ,zikhala bwino ,Yehova alipo.

25/08/2022

He is a Lord,he is our savior

08/05/2022

Padutsa Zaka khumi dziko lamalawi lilibe mtsogoleri potsatira imfa ya emwe adali mtsogoleri nthawi imeneyo Malemu Bingu Mutharika.Mwina Azasankha mtsogoleri wina mu 2025

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Kabula?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Blantyre
Kabula
BANGWE