Joy your time

Joy your time

Share

Health/beauty

29/01/2024

Osadandaula ndi January akuthano komaso ndava kuti February amuonjezera masiku azithera 31 ine eeh kumeneko kusitha kwa nyengo kapena chani

06/03/2022

Nkhani zoti mulungu alinafe koma ndiyona coz tsiku lomwe tikujoyali azathu ena atsikira kulichete ena ndye tisachite kunena koma mulungu ayi alinafed

03/03/2022

Muthu ukakhala m maluzi ndye abea ako akukufulasher koma maunitsi ulibe umazatchecker balance mu card ngakhale ukudziwa kt mulingogole kenako umapita ku acount ya airtel money ngakhale ukudziwa kuti sudayikeko ndalama koma uma checker balance hoo mukufuna chani kwenikweni

03/03/2022

Koma zina ukava kamba akunga mwala eti banja lina lomwe lidali ndi ana atatu amuna awiri wamkazi mmodzi ndipo tsiku lina atatha kudya mwana wamkazi adamasuka ndikuuza makolo ake kuti iyeyo ndi m,bale wake anganiza zoti akwatirane

Like our pange kuti muve zambiri with Aubrey Bemah. (The gaguness)

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Dedza
Lilongwe