Azimayi A Single 265
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Azimayi A Single 265, Health/Beauty, Lilongwe.
22/04/2023
02/03/2023
Hello Malawi Finest Singles
Pali mkazi wa zaka 32 ndimakhala ku Blantyre. Ndili ndi mwana mmodzi and ndili pantchito (financially stable) ndikufuna mamuna wa serious wa banja. Akhale mamuna yemwe ali ready kulowa banja, at least wamwana tizizalelera limodzi. Oyambira zaka 33 upwards. BTW my name is Beatrice
Whatsap 0992201273
27/02/2023
Morning guys ,. Thu beautiful lady is looking for a serious relationship her name is shirah ,,she is a malawian amakhala Ku cape town,,,she is working Ali ndi mwana mmodzi basi koma alibe mwamuna,,,she wants a serious man to settle down with ,,,,koma akhale osachepela dzaka 30 ...
0992201273 for more information
16/02/2023
Am a women aged 33 ndili ndimwana mmodzi.
,not working ndimapanga business ndikufuna mamuna waserious ofuna banja .Ine ndimapezekera ku Lilongwe koma kwanthu mkukhotakota.
0992201273 inbox
12/02/2023
Ndine bambo wazaka 40 pano ndili ku mzimba komwe ndikugwira ntchito ya boma.mkazi akhale woyambira zaka 30-38 yemwe kusukulu adapitako komanso akugwira ntchito ngati lawyer,teacher,nurse or soldier.wa ana awiri kutsikira pansi vuto palibe chifukwa ine ndili ndi mwana mmodzi.
12/02/2023
Ama man aged 44 single and with three kids, my type of woman should be understanding church going low self esteem and black beauty nice figure as well beauty inside and out side thanks
11/02/2023
Hello Malawi Finest Singles
Ndine mkazi wa zaka 30 ndimakhala ku Blantyre. Ndili ndi mwana mmodzi and ndili pantchito (financially stable) ndikufuna mamuna wa serious wa banja. Akhale mamuna yemwe ali ready kulowa banja, at least wamwana tizizalelera limodzi. Oyambira zaka 33 upwards. BTW my name is Tamika
Whatsap 0992201273
06/02/2023
Inbox for more information
Hello mummy
Ine Leah waku lilongwe ndufuna mamuna wa serous wabanja ndili ndi zaka 21 ndilibe mwana panopa ndikungokhala Kaye koma ndili ndi msce. Mamuna ayambire 26 wa serous osati time waster ai.
Aka ndika black natural beauty only serous guys
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe