GRAND VOICE YM2
Grand voice sound
11/10/2022
Nthawi zina ndibwino kumayamikira zinthu zikakhala bwino
Ndiye ine ndimati nditele kuti
Iyiyi ndi couple mbambande ,
Prophet Shepherd Bushiri ndi Bushiri amakhala mmoyo osangalala mu nchikondi Chao, malingana ndi momwe ndimaonera tiyeni ku comment section tipange post tili ndi achikondi athu π
03/07/2022
π²πΌ
Pomafika chaka chΓ‘ mawa
Nafe tifika apaπ΅pa matrllion pepala limozi
Ndiye kuti tikhala olemela thonseπππππ
Osaiwala kupanga LIKE Page π
Theba yafikano
Poyaluka Nanga izi ndi zichani
π
Osaiwala kupanga LIKE Page
SOUTH AFRICA πΏπ¦
President ramaposa Walesa kuvala
Mask π akuti Corona watha
Ndiye wina and palamule dΓ‘la siulowa muno opanda mask
Undinva cha munsa mtalowa kale
Osayiwala kupanga LIKE Page π
MUTIUZA BWINO
ZITHEKA BWANJI BLACK OUT THE WHOLE MALAWI π²πΌ????????
15/06/2022
Ntchito ndi zambiri
Nanga uncle wa amagwira ntchito yanji?????π€£π€£π€£π€£π€£π€£π€£π€£π€£
Osayiwala kupanga LIKE Page π
14/06/2022
OZIWA MWAZIWA TIUZENI MUTI CHANI??? ππππ
09/06/2022
CHENJEZO β β β β β οΈβ οΈβ οΈβ οΈ
ENA MUKUTSUTSA. NANGA IZI
NDALEMBA NDINE
NOTED
OSAYIWALA KUPANGA LIKE PAGE π
09/06/2022
CHENJEZO β β ββ οΈβ οΈ
MAWA PA 10 JUNE FRIDAY
THEBA YONSE KUWILILA
NDI ZIWONETSELO ZA KUKWELA KWA MITENGO YA KATUNDU KUPHATIKIZA PONSO. PETRO
CHONCHO AMENE TIMAGWRA NTCHITO MUTALI MUTALI TIKUFUNIKA KUYENDA MOSAMALA KAPENA OSAPITA KUMENE
PA CHIFUKWA CHOKUTI A NZATHUWWA AKAMAPANGA ZIWONETSELO AMAFUNA ALIYENSE ASAGWIRE NTCHITO NDIYE AKAKUWONA ZOTI UKUGWIRA AAMASIYA ZAWOZO NKUYAMBA KUPANGA ZAIWE POWONA NGATI UKUDELELLA MALAMULO AWO
Noted
Osayiwala kupanga LIKE Page π
07/06/2022
MALAWI π²πΌ
BOMA LA MALAWI LALANDILA STIMA YAPAMADZI KUCHOKELA KU CANADA π YOMWE IKUYEMBEKEZZEKA KUZAFIKA KU MALAWI π²πΌ. MWEZI WA NOVEMBER 2022
FUSO NKUMATI SITIMA IKULILENJI
KODI I ZIYENDA NYANJA YAKE iti?????
DON'T forget to like page
Click here to claim your Sponsored Listing.
Contact the business
Telephone
Website
Address
Lilongwe