Kubweza Ndata

Kubweza Ndata

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kubweza Ndata, Health/Beauty, Lilongwe.

20/03/2024

MACA PLUS MAMBA

13/08/2023

WAKALAMBA WAFUNA
Tikupezeka ndi moringa oil, m***a kugwilitsa ntchito moringa oil poika mafuta odzola malo mwa glycerin.Ndipo amabwezeletsa mchimake thupi lanu kuoneka lochitsa kaso

24/07/2023

Mthenda ya likango ndi yochititsa manyazi makamaka vutoli likakhala ndi munthu wamkazi😓 Likango likafika pomela zimakhala zochititsa manyazi kwambiri kuti munthu akhale omasuka kuchipinda🙆 Pezani virgo herbal powder kuti m***ane nalo likango

24/07/2023

Ameneso mwakwapuka ndi chindoko kapenaso mabomu m***a kupeza wanu Virgo herbal powder kuti muchile kumatendawa

Kubweza ndata 31/05/2023

Kubweza ndata WhatsApp Group Invite

28/05/2023

Kubweza Ndata Health/beauty

18/05/2023

Ma herbal products othandiza matenda osiyasiyana tili nawo kuma office athu.Tiyimbileni phone pa 0997278832 kuti mudziwe zambiri

18/05/2023

Azimbambo ofooka osapita kogona musanadye thochi ndi water melon🙌

29/04/2023

Ngati amangokusisitani 😓 Tsiku lina dzapatseni thochi ndi watermelon kuti adye ngati ka fruit after meal musanapite kogona, usiku umenewo simudzagona😂😂😅

29/04/2023

Pewani kumwa zakumwa zozizilitsa kukhosi zomwe zili ndi sugar wambiri kuti mukathe Kuthamanga bwino liwiro.Yemwe amadziwa mkonya wamva

24/04/2023

BWEZANI NDATA KUTI KHUMBO LAWO LIKWANITSIDWE
Mwa amuna 10 omwe amafusa zama products anthu. Amuna 8 amafusa zokulitsa chida pamene awiri amafusa za Mankhwara opeleka mphamvu kuchipinda.

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Lilongwe