Male And Female Clinic
We have got natural health supplements that treat more types of disease.
08/05/2025
PAMENE IPHYO YASIYA KUGWIRA NTCHITO YAKE BWINO.
(KIDNEY FAILURE)
Iphyo ndi chiwalo chofunikira kwambiri mu thupi lathu. Munthu wina aliyense Ali ndi ma kidneys awiri omwe ntchito yake ndi kuchotsa zoipa mthupi kudzera mu mkonzo. Iphyo imasefa magazi kuchotsamo zoipa makamaka michere ina yoipa ndi zotsalira za mankhwala komanso zakudya zomwe timadya.
Iphyo imachotsa madzi ena mmagazi kupangisa blood pressure kukhala ya mlingo oyenerela. Magazi athu kuti apangidwe, michere ina imapangidwa ndi iphyo kuti izi zitheke.
Pamene iphyo yasiya kugwira ntchito yake zinthu zonsezi zimavuta kuti zitheke nkubweletsa mavuto ambiri mthupi lathu omwe amaika moyo pachiopsezo.
Mmbuyomu nnafotokoza po za mmene tingasamalire iphyo yathu popewa ma Khalidwe ena monga kumwa mowa moonjeza, kusuta fodya, kumwa Mankhwala ena mosatsata malangizo oyenera. Kuzimanga Pamene tili ndi chilakolako chokakodza komanso kukanika kupeza thandizo loyenera tikadwala matenda a mchikodzodzo Pamene munthu uli ndi Vuto la chiwindi komanso mtima chiopsezo chokhala ndi Vuto la iphyo chimakwera.
Mwa zina kuti iphyo isiye kugwira ntchito nthawi zambiri nchifukwa cha zinthu izi:
1)pamene tizilombo ta ma bacteria tafika mu iphyo ndipo sitinapeze thandizo msanga.
2)chifukwa cha matenda a sugar Pamene thandizo lachedwa kapena sikupangidwa control.
3)makhwala a mu gulu la aspirin monga diclofenac, brufen, indocid Pamene tikumwa mowilikiza.
4)Pamene misempha ya mu iphyo yaonongeka ndi kukwera kwa blood pressure.
5)Pamene mu iphyo mwapezeka timibulu (kidney stones)
6)Pamene tataya magazi ambiri komanso ngati madzi achepa mthupi.
Izi ndi zina mwa izo komano tingadziwe bwanji kuti iphyo yathu sikugwira bwino ntchito?
Ngati mwaona zizindikiro izi chonde pitani kuchipatala msanga nkutheka ndi Vuto la iphyo:
1)kukodza mkodzo ochepa kapena kusiya kukodza kumene.
2)kutupa kwa mapazi komanso kumamva kulemera mapazi poyenda
3)kumva kuwawa molumikizana mafupamu komanso kutupa
4)kufooka komanso kupuma mobanika
I
08/05/2025
*HEART DISEASE*
*MAVUTO OKHUDZA MTIMA*
👉 *Tinvetse pano Kuti Mtima ndi Chiwalo chofunika kwambili pa thanzi la munthu munthu aliyense, Pachifukwa ichi Mtima ndi ofunika kwambili kuwudziwa bwino komaso kudziwa ntchito zake komaso kudziwa zomwe tingachite Kuti tidzitha kuwuteteza pa zovulaza zili zonse zomwe zimakhudza ntima*
⏩ *Mtima kwambili umagwila ntchito zopopa magazi Pogwilitsila ntchito mphweya wa oxygen Kuti magaziwo azitha kuzungulila ziwalo za thupi lonse cholinga Kuti tikhale ndi moyo komaso moyo wathanzi Ndipo chiwalochi chikangofoila ndikusiya kugwila ntchito yake moyonso nawo umathela pomwepo*
*↪️ Ngakhale zili Chomwechi Kuti chiwalochi ndi chofunika kwambili pa thanzi lathu nthawi Zina chiwalochi chimatha kukumanaso ndi Mavuto omwe Amayambitsa matende mitundu ingapo*
*Tatiyeni Tikambilaneko zinthu zingapo zomwe zimayambitsa matenda okhudza ntima*
1. kunenepa kwambili
2. Kumwa mankhwala achizungu Kwa nthawi yaitali
3. Kumwa zoledzeletsa mwa uchidakwa
4. Kusuta fodya
5. Kusapanga masewela
Gulani BAZOOKA IMMUNITY BOOSTER pamtengo wosaboola mthumba lero. Moyo nkamodzi!
*BP*
*High blood pressure* imadziwikanso kuti *hypertension*
*Hypertension* *-imayamba ngati mtima wayamba kupopa magazi ambiri kuchokera kapena kupita mu njira* *zing'onozing'ono*
*Kusalandira* *magazi kapena kulephera kupititsa magazi okwanira ku ziwalo ndi kumene kumapangitsa* *Hypertension* *kungolongosola mwachidule chabe*
*Choophya kwambiri pa nthendayi ndi chakuti nthawi !zina umatha kukhala ndi nthendayi koma osaona chizindikiro chilichonse choti uli ndi* *hypertension*, *ndipo nthawi zina nthendayi imatha kungofikira kuononga ubongo wathu, mtima, maso athu* *komanso imphyo
Komabe titha kuzindikira* *mwachangu kuti tili ndi* *hypertension* *ngati tili ndi zoyezera bp ndiponso tizidziyeza pafupifupi, ndipo tikaona kuti bp yathu ikumakhala yokwera mobwerezabwereza pamenepo tidziwe kuti tili ndi vuto la* *hypertension*
Kuopsya kwina kwa *Hypertension* *ngati sitikudziwa kuti tili nayo kapena tikuona zizindikiro zina zavutoli koma timangonyozera zotsatira zake timatha kukhala ndi vuto la mtima* (heart attack komanso stroke)
Kunena zoona* *hypertension* *kuchipatala kumakhala kovuta kwambiri kuti munthu achire *BP* koma kuti kuchipatala amangopereka zongoziziritsa chabe, moti anthu ambiri amatha kuyamba kumwa mpaka kumwalira akumwabe mankhwala a kuchipatala a BP koma osachira.*
*KWENIKWENI CHIMAYAMBITSA BP NDI CHANI*
*Hypertension* ili mmagulu awiri
1) primary hypertension
2) secondary hypertension
*Primary hypertension*
*-Iyi imayamba chifukwa cha *genes*,* *kumene tabadwira kapena ku mtundu wathu ngati kuli* *winawake anadwalapo BP pali kuthekera koti ena mwa ana obadwa kutsogoloko pa mtundu wanuwo amadzakhala nawo ndithu*
*Primary hypertension* *munthu amatha kuyamba kudwala chifukwa cha nyengo yomwe iye ali posatengera kuti kwawo munthu wina anadwalapo BP kapena ayi*
*Secondary hypertension*
*-Iyi imayamba chifukwa cha Nthenda yochokera mu imphyo mavuto ena a mtima *Mankhwala ena a kuchipatala ali ndi kuthekera* *koyambitsa BP
Kumwa* *mankhwala a kuchip
*KHANSA YA PA KHOSI (THROAT CANCER)*
*_Khansa ya mtundu uliwose imavala dzina kutengela ndi malo amene yayambila, ngati ndi pa nkhungu ndiye kuti imatchedwa khansa yapakhungu ngati ndi mmagazi imatchedwa khansa ya mmagazi ngati ndi mmafupa imatchedwa khansa ya mmafupa ngati ndi khomo la m'chibelekero imatchedwa khansa yakhomo la m'chibelekero etc_.*
*ZIZINDIKIRO*
-Kuvutika/kukanika kumeza zakudya.
-kupweteka kwapa mtima
-kuluza weight
-kusasa mawu (hoarseness)
-kusanza
-kukhosomola kosatha
-chimbudzi chakuda (black stools) zomwe zimadza chifukwa Cha magazi amene amatsikila mmimba.
-kuva ngati pakhosi payala chinthu/Pali zilonda kwa nthawi yaitali
-chidikhodikho chosalekeza
*∆ Zizindikiro pa izo zokha sizokwanira kuti mungaziganizire kuti muli ndi cancer pokhapokha achipatala atatsimikiza*
*KUPEWA KHANSA YA PA KHOSI*
✓ pewani kumwa ndi kudya zinthu zotentha kwambiri monga tea (imwani ali kamulingo kabwino komweka)
✓ pewani kumwera ndi kudyela zinthu zotentha mu cup/mbale za plastic.
✓ pewani kumwa madzi ozizila kwambiri.
✓ Ngati ndinu oyimba, onetsetsani kuti mukuimba kukhosi kwanu kuli kofewa (kumwa madzi pafupipafupi)
✓ pewani kuimba/kukuwa/kulira motulutsa mawu kwanthawi yaitali
✓ pewani ma X-ray ambiri apa khosi ndipa mtima
✓ ngati muli ndi vuto la gas komanso acid reflux onetsetsani kuti mwanjila iliyose mukulandila thandizo lamavuto amenewa
✓ siyani kusuta fodya
✓ Chepetsani mowa
*CHENJEZO*
*∆ Kuchipatala kulibe mankhwala othetsa khansa, njira zonse zimene odwala khansa amathandizilidwa ndizongoonetsetsa kuti khansa yo sikupitilira kufalikila komaso kupha ma cells amene akhudzika kale ndi cancer yo koma izi sizithana ndi choyambitsa khansa*.
*🪸 musaluze Moyo ndi nthenda yoti m***a kuchira ai choonde.*
*Koma ndi njira zachilengedwe, palibe matenda amene alibe mankhwala*
_Cancer free is our favorite_
13/03/2024
INFERTILITY POSSIBLE SOLUTIONS
Challenges getting a child has various causes, like
▪︎Infections,
▪︎Hormonial problems,
▪︎Blocked tubes,
▪︎Endometritis,
▪︎Ovulution problems,
▪︎Cysts
▪︎Fibroids ,
▪︎Pid
▪︎Pcos
▪︎Uterus problems,
▪︎Male related issues.
We full fertility screening and consultation to determine what is delaying one not to get a child and give the right medications, to help one conceive faster without complications.
WE CAN HELP AND WE CAN'T WAIT SEEING YOU TESTIFYING AND THE PAIN WILL GO.
13/03/2024
HOW TO DESTROY AND SHRINK FIBROIDS WITHOUT SURGERY:
Many people who have uterine fibroids don't have any symptoms. In those who do, symptoms can be influenced by the location, size and number of fibroids.
The most common symptoms of uterine fibroids include:
✓Heavy menstrual bleeding or painful periods.
✓Longer or more frequent periods.
✓Pelvic pressure or pain.
✓Frequent urination or trouble urinating.
✓Growing stomach area.
✓Constipation.
✓Pain in the stomach area or lower back, or pain during s*x.
Fibroids Treatment:
We've a combination of high Quality products that destroys uterine fibroids and shrinks the blood vessels that feed them without undergoing any surgery or regrowing back and make your uterus more fertile.
Surgery/ operation can't give u permanent solution because the scar tissue left can lead to INFERTILITY or turn cancerous or regrow again.
WhatsApp me now by coming to my inbox
13/03/2024
👉👉 ACIDS AND ULCERS 👈👈
🔘Acids sometimes are called Heart burn , Although there is nothing to do with heart.
🔘Acids occurs when stomach Acids moves up to the Oesophagus,(hydraulic Acids in the stomach),
🔘Oesophagus is designed to take down food only, not to regurgitate
🔘Some of the causes of acids is:
🟡Stomach disorders like Hernia and too much toxins, comes from food we eat or beverages .
✍️Obesity can also causes Acids ,you start to feel a heart burning, because of too much fat accumulates in the stomach disturbs breaking down of food.
✍️Some certain types of food like:
1️⃣Caffeine, 2️⃣Onion, 3️⃣Alcohol are the causes of this tragic ,irritating diseases.
🔥So, we provide 💯% natural and organic products which work in combination to , Detoxfy your digestive system to restore normal secretion of stomach Acids and also to make oesophagus resistance
🔥They also burn internal fat,and convert it to energy.
🔥These products make the diaphragm to move in a normal way hence avoid uplifting of Acids back to The throat.
🔥These products they even Heal, Ulcers, Constipation,piles, gastritis e t c
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Address
Lilongwe