Kuwala Optics

Kuwala Optics

Share

Optical and eye care services. High quality at low cost.

03/06/2026

ONE ONE

Azibambo, ku left side.
Azimayi, ku right side.

Uku mmodzi, ukonso mmodzi, aweruke ndi Kuwala Package 😊

Ponyani any comment, koma tag your friends to like your comment. The comments with more LIKES win the Kuwala Packages 🥳

Kugula timeneti mtengo wake ndi K89,000 only, full package 😊

[No zigoba accounts. You can tag as many people as you want]

Photos from Kuwala Optics's post 25/05/2026

LADIES INUYO 🙌

"Ine ndikufuna frame ya Thick, yokhala ngati Butterfly, koma ikhale ya Blue. Not Blue as in Blue, koma Blue opitira ku yellow yellow chonchi."

Awawa chabwino K85,000 only, full Kuwala Package 😊

Photos from Kuwala Optics's post 17/05/2026

NEW STOCK

Available in all our shops.
Prices: K55,000 to K95,000

Pamenepo ndekuti full Kuwala Package, momwe muli zinthu izi;
1. Frame
2. Lenses
3. Spectacle case
4. Lens cleaner
5. Lens wiper

Omwe talembapo kuti Limited ndekuti abwera kale ochepa.

Kuyeza maso ndi ulere. Ma glasses amakhala ready same day.

[Premium and Executive frames available]

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.

Call/Whatsapp: 0990511960

14/05/2026

KAMUZU DAY
👓
Open 08:00 am
Close 02:30 pm

Photos from Kuwala Optics's post 04/05/2026

TRANSPARENT FRAMES

Promotion yama frames a Transparent kapena White ikupitilira, pomwe taika massive K15,000 discount on any transparent/white frames. 😊

Komanso ma frames ena onse ali ndi discount ya K10,000. (See pictures on previous posts)

Promotion until 09 May.

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, Opposite AXA
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.

Call/Whatsapp: 0990511960

01/05/2026

LABOUR DAY
👓
Open 08:00 am
Close 02:30 pm

28/04/2026

HUSTLER'S LOOK

Panopa ititi ukumabwerako ndi Change chokwana K10,000 😊

Ndi Promotion ilipoyi ya Double discount, ititi tachoka pa 89,000 kufika pa 79,000. Ndekuti 10 pin kubwelera pathumba.

Pena mpaka K15,000 kubwelera pathumba, maka mukasankha transparent or white frames. 😊

[You never know, wina titha kumuvungira kameneka azatenge]

Photos from Kuwala Optics's post 21/04/2026

DOUBLE-DISCOUNT PROMOTION

(Up to 09 May)

Kulandira ma discount kawiri 🥳

Yoyamba ndi K10,000 discount. Iyiyi yaikidwa pama glasses ena aliwonse 😊
Yachiwiri ndi K5,000 discount. Iyi ikupanga apply pama glasses (frames) a transparent or white 🥳

Prices: K49,000 to K79,000

Kuyeza maso ndi ulere. Ma glasses amakonzedwa pompopompo.

[Premium and Executive frames available]

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.

Call/Whatsapp: 0990511960

20/04/2026

ZIMWEMWE

Koditu sanachedwechedwe, mawa lake anali atafika kale kuzatenga Prize yake ya Kuwala Package ku Area 25 shop 😊

Matilda Bula Luhanga mwawala kwabasi, after kusankha ka Emerald Green 🔥

15/04/2026

CONGRATS WENIWENI 🎊

Tinathiridwa mphepo ku inbox, kuti bwanji comment ya 81 Likes taijowa. Abale tinaiwala kuvala ma glasses, comment ya Matilda Bula Luhanga osaiona olo 😁

Congrats Matilda, zatengeni full Kuwala Package yanu muwale 🎊

PS: poti Greatness Mandala tinamulengeza kale, abwerebe azatenge (frame + lenses) akawale naye.

Congrats girls 🎊

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Area 2
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:30
Tuesday 08:00 - 16:30
Wednesday 08:00 - 16:30
Thursday 08:00 - 16:30
Friday 08:00 - 16:30
Saturday 08:00 - 14:00