John nkhoswe
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from John nkhoswe, Health/Beauty, Mandala.
21/01/2026
*TIPEMPHERE🧎♂️*
``` Ulemu ndi matamando zipite kwa Inu Yehova Mulungu wanthu chifukwa chotilora ife ana Anu kudzukaso ndi moyo mu tsiku lalero,tikuti zikomo.
Pozindikira kuti ndife anthu wochimwa tikupempha kuti Mutikhululikire zochimwa zathu tonse pa group pano ndi tikupempha kuti Mutitsogolere mu zochita zathu zonse kuti tikachite mu ulemelero Wanu.
Pali ena amene sanadzuke bwino akudwala Ambuye tikupempha kuti Muwakhudze ndi dzanja Lanu lamachiritso.Olira Ambuye tikupempha kuti Muwatothoze,anjala Muwadyetse Ndinu Yehova komaso pali ena ali ndi mavuto osiyanasiyana onse Ayendereni mwa zosowa zawo.
Mwapadera Pitilizani kuti tsogolera mu zonse kuti ngati nkotheka maina athu adzapezeke mu buku Lanu la moyo pamene Mukubweranso posachedwa kudzaweruza ndikoli.
Inu Mukule ife tichepe, tapempha zonse mu dzina la Ambuye wanthu Yesu Khristu```
*Amen🙏🏻*
18/01/2026
Zolozolo bag dad teaching
04/04/2022
04/04/2022
Mmmmmm
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Mandala