Lazaro stezzoh

Lazaro stezzoh

Share

New comedy videos

19/10/2022

Mumafila uti pa onsewa kwa amene mumaxsata za music

Profile pictures 16/06/2022

MWANA NDI BAMBO AKE AGWIDWA NDI CHAMBA

aPolisi ku Ntchisi agwira bambo Zakalia Nyirenda azaka 56 Komanso mwana wawo Lufeyo Zakalia wa zaka 24 chifukwa chopezeka atalima chamba.

M'neneri wa polisi ku Ntchisi Yohane Tasowana watsimikiza za Nkhaniyi ndipo wati awiriwa agwidwa dzulo pa 15 June m'mudzi mwa Kafulu T/A Chilooko m'bomalo.

ATasowana ati patsikuli apolisiwa adatsinidwa khutu ndi 'anyapapi' ena ndipo apolisiwa atathamangila kumaloku adakwanitsa kuzula mitengo 945 ya chamba yomwe ati ayitumiza ku Chitedze Research Station kuti akayipime.

-Naomi Kamiza

Profile pictures 16/06/2022
Photos from Lazaro stezzoh's post 11/06/2022
20/05/2022

Moni amalawi ine mwana wanu mwaambuye ndabweranso ndinkhani yoti"""" khalani pompo mumve

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Mulanje?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Mulanje