Royal Crest Poultry
let us talk about it ๐
Turkey ๐
29/01/2026
Mikolongwe eggs available hit up.
Hamble beginning ๐
21/10/2024
Ex bodyguard of pdiddy claims Diddy poisoned Jamie Foxx " well I know he poisoned Jamie Foxx and Jamie reported him to the FBI and that's a fact"
๐ณ
21/10/2024
Bwalo la milandu ku Ntcheu lalamula bambo wa zaka 30, a Innocent Nahipa, kupereka chindapusa cha K500,000 chifukwa chozemba kulipira msonkho pa chipata chogulira njira chapa Chiingeni mu mseu wa M1.
Mboni ya boma, a Thomas Lucio, inauza bwalo kuti a Nahipa anapalamula mlanduwu pa 25 September chaka chino.
A Lucio anati pa tsikulo a Nahipa amayendetsa galimoto la Honda Freed nambala yake CZ7383 ndipo anazemba kulipira podutsa pachipatachi limodzi ndi galimoto Lina lonyamula katundu.
Ataonekera kubwalo la milandu, a Nahipa, omwe ndi akwa Ntonya T/A Nsamala ku Balaka, anawapeza olakwa choncho iwo anapempha bwalo kuti liwachitire chifundo kaamba koti ali ndi udindo osamala banja lawo.
Koma oweluza mlandu, a Alleyab Imani, anati apereka chilango chokhwima pofuna kupereka phunziro kwa oyendetsa galimoto omwe amadutsa pa zipata zogulira njira mu mseu wa M1 mdziko lino.
Source: Kelvin Phiri
21/10/2024
Don Jazzy did not take it lightly with Oluwadolarzโs recent accusations about the music industry and its involvement in homosexualism. Full details in comments.
21/10/2024
Anthu ambiri, kuphatikizapo ma membala a chipani cha Malawi Congress (MCP), asonkhana pa bwalo lamasewero la Nyambadwe munzinda wa Blantyre kumene kuli mwambo wa maliro a Mabvuto Chimwaza, amene anali wapampando wa achinyamata m'chipanichi ku Ndirande.
Malemuwa anapezeka atafa kuseli kwa nyumba yawo ku Ndirande Loweruka mmawa.
Anthu amene ali pamalopa ali ndi nkhope zachisoni ndipo akuona nkhope kuti apereke ulemu otsiriza
21/10/2024
Today!
12/07/2024
Livingstonia water source ๐
kukakha dancehall opanda zaza
take it easy as it goes...
Click here to claim your Sponsored Listing.
Website
Address
Mzuzu