Chingoni Dickson

Chingoni Dickson

Share

Dude signs electronics

12/11/2024

Sweet home sweet 🤣🤣🤣🤣🤣

12/05/2024

Onerani comedy ya khoswe mwano done by ineyo

18/04/2024

Kodi munandiuzapo mnene mumanvera mukamandiona ❓ ngat mumandiona kt ndine wamatama ndifikiren pafup ndipo muone mnene ndiliri

13/10/2023

Malawi has been devaluated......

12/09/2021

Kukumbukira tsiku lomwe unabadwa sibwino kumasangalala kma kumalira chifukwa zaka zokhala ndi moyo zimakhala zikuchepa ........inu mukuti. Bwa

12/09/2021

SIZOPHWEKA KUKHALA MUTU WA BANJA

ZiMAFUNIKA KUKULA NDI MZERU

Profile pictures 11/09/2021

Zingayambe kuyiwalika nthawi imeneyo He E wa munthalika with madam munthalika....Zidali zinthu zosangalasa kuwona mtsogoleri wanthu akumanga ukwati
Rlp to Our president wa munthalika
Don't forget to like Our

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Namadzi
Zomba