Zokoma malawi
����������
Happy Sunday to all
20/01/2023
Usaziyike pa pressure
Success yawo yisakupase mpanipani!
Hello North people Ndikuziwa Kaswili yemwe anayimba nyimbo iyi mukumuziwa ndithu .
Apa watulusaso video yake yabwino kwambili Akuti
Tremour Ndidolo ndipo saphwekesa
Tiyeni tose tiywonerere Video yobeba uyi monga mwanthawi zonse
Check this 👇
OLO_Official Music Video 👉https://youtu.be/BiA7kUE3aYQ
Audio👉 https://mikozinet.com/id/olo-prod-drue/
https://umathadaily.com/tremour_olo/
Ulemu wako aise umabebesa sound
Gayezi please follow my pege and god bless you 🥺🥺 Malawi 💪
18/01/2023
Adaawawa amatha kuyimba kwambiri nyimboza ke mukhoza kupanga Download is Nice song 🔥🗣️🗣️ https://flameworks-entertainment.com//song.php?id=32s
17/01/2023
Cacoon x Teddy athu wa akut akufanana kwambili ndizowona muwone nokha kmaso ndipachibale pawo 🔥🔥 ayimbaso limozi 🎵🙏🙏
Teddy Makadi auzeni athu aziwe za ubale wathu Asama kayike coz sitikusiyana kwambiri wona brother So ma guys woneraniko m ,Malele link ndi iyiyi music video 🔥💝💝💝 https://youtu.be/DKRw5rt-XDc?si=GHqyTrtS8Mtrgeew
16/01/2023
We are on, Mesa Video finally out. Your support will be highly appreciated. 2k views in 24 hours.
Link:
Pop Young - Mesa [Official Music Video] Pop Young - Mesa Stream: https://distrokid.com/hyperfollow/popyoung/mesaDownload: https://mikozinet.com/artist/pop-young/Follow Pop YoungFacebook: https://ww...
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
���
Zomba