ChigweMalawi

ChigweMalawi

Share

People to be remembered in africa

22/12/2024

Iwu ndi msapha omwe mayiko akunja apanga pofuna kukhaulisa malawi kamba kagawo lomwe Malawi yatenga ku nkhondo ya ku Ukraine komanso Gaza, kumbuyo kwa Tanzania kuli mayiko omwe akufuna kukhaulitsa Malawi ๐Ÿ˜ฎ

08/12/2024

With Manchester City โ€“ I just earned their Top Cityzen badge!

18/09/2024

Genius๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

11/09/2024

Kina phiri titengeni bas๐Ÿคธ๐Ÿ™‚๐Ÿค“

11/09/2024

Mabedi wati tilibe tsogolo mu AFCON

Mphunzitsi wa timu ya mpira wamiyendo ya dziko lino, Patrick Mabedi, wabwera poyera kuti pakhala povuta kuti Flames idzipezere malo mu ndime yotsiliza ya mpikitano wa 2025 Africa Cup of Nations (AFCON).

Mabedi walankhula izi atagonja 3-1 ndi timu ya Burkina Faso usiku wathawu ku Bamako, m'dziko la Mali.

"Zikhala zovuta kuti zinthu zitiyendere poyang'anira kuti tiri kumapeto opanda pointi iliyonse. Anzathu zawo zikuyenda ena ali ndi mapointi anayi ena atatu, ife tiribe pointi," watero Mabedi.

Malawi ilibe pointi iliyonse pamasewero awiri omwe yasewera mugulu L lomwe Burkina Faso ndi Senegal akufanana mapointi omwe ndi anayi potengera kuti angosiyana zigoli zomwe achinyitsa komanso zomwe agoletsa.

Burundi ili panambala yachitatu ndi mapointi atatu omwe anatolera atagonjetsa Malawi, pamasewero omwe analipo sabata yatha pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe.

Wolemba: Richard Tiyesi


Timveni Online ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผโœ๐Ÿฟโœ๐Ÿฟโœ๐Ÿฟ

11/09/2024
11/09/2024

๐Ÿค‘๐Ÿค“

Month end ๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚ with baby mama

11/09/2024

๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

07/09/2024

I don't want to die alone ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Thondwe
Zomba