HoneyMoon Mlw

HoneyMoon Mlw

Share

Sole authorised distributor of all Honeymoon products,with direct access to the product manufacturers

03/11/2024

ENERGY DRINK
Ali ndi vitamin B6 komanso vitamin B12 wambili amene amathandiza kuchepetsa ululu waminofu.
Nyamakazi yonse balala!!!!
- achinyamata komanso azibambo amene muli ndi vuto lothira mwachangu bwerani katundu wanu ndi ameneyu
- achinyamata kapena azibambo amene mukathira mumakanika kubwereza round ina, bwerani changu
- azimayi nanunso amene thupi linazizira ndipo daddy akamakugwirani mumakhala ngati chiyabwe chikukugundani, come over.
Kungosungunula ka sachet konse mu botolo la madzi la half litre ndi kumwa. Results after 2 hrs... Kenako muzandiuze ndinu kuti game inatenga macdays angati.
Found in Kawale Lilongwe. Kutali timatumiza.

03/11/2024

ENERGY COFFEE
mwini filimu
Bwenzi la nyengo zonse.
Salephera. Safowoka. SatopetsaπŸ’ͺπŸ’ͺπŸ’ͺ
Ndi kofi osakanizidwa ndi zitsamba monga Ginseng, tokart ali, cinnamon ndi zina zotero.
Eyetu. Ntchito yake ndi mtukula kuchipinda.
Onse amuna ndi akazi akhoza kumamwa kuti azithandizana ku chipindako.
Amuna amene muli ndi low s***m count, amathandiza kwambili kupanga boost s***m quantity and quality yanu.
Azimayi amene mumamva kuzizira ku nkhani yaku chipinda, amatenthetsa thupi ndipo daddy adzaona kusintha.
Highly recommended to couples who want to conceive.
Mwanamizidwa kokwanira. Bwerani muzagule katundu weniweni
Mukazengereza ndi zanu mukadzimvera kwa a neba kowonera Arsenal πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

03/11/2024

HONEYMOON HONEY HERBAL MIX PASTE.
For both Men and Women
Mmenemu mudzapezamo achina Ginseng, turmeric, ginger, cinnamon, black cumin, mecca rose tea, myrtle ndi zina zambili zothandizira kuti misempha yanu ikhale yotseguka bwino ndi cholinga choti magazi aziyenda bwino mthupi mwanu.
Amene muli ndi mavuto monga;
- kufowoka ku nkhani zakuchipinda (nyere yochepa)
- amene muli ndi vuto la low blood pressure/high blood pressure
- stress imakusowetsani mtendere.
- muli ndi shuga ndipo kuchipinda zikumavuta
- muli pa ART treatment and kuchipinda zikumavuta
- amene muli ndimisempha yoti idatsekeka
- nonse amene Kuchipatala adakupezani ndi vuto la low testosterone levels

PRICES:
HONEYMOON HERBAL MIX sachet K5,000. Order box of 10 sachets K40,000
HONEYMOON COFFEE sachet K5,000. Order box of 5 sachets K20,000.
Energy Drink K4,000 sachet. Order box of 5 sachets K20,000
USAGE:
HONEYMOON mix paste, nyambitani uchi onse umene umakhala mu sachet. Results after 2 hrs. Maximum 2 sachets per week.
HONEYMOON COFFEE, Sungunulani coffee yense wamu sachet mu cup yamadzi otentha. Sugar or no sugar. Instant results. Maximum 2 sachets per week.

CONTACTS:
Kawale 1 Near Police
0992330756 whatsapp or call
Bwerani muzamuyese katundu ameneyu.
Mukazengereza mukazimvera kwa a neba kowonera Arsenal πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

HoneyMoon Mlw Sole authorised distributor of all Honeymoon products,with direct access to the product manufacturers

Photos from HoneyMoon Mlw's post 03/11/2024

Everyone deserves a quality life. Why stress yourself while honey moon is under your pillow?
Finally honeymoon products are in Malawi.
Contact us now.
0992330756
We send everywhere in Malawi and neighbouring countries

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Zomba