Pido International

Pido International

Share

HUMAN RIGHTS ACTIVIST
FOUNDER OF PIDO INTERNATIONAL ORGANIZATION
HEROS AWARD WINNER OF HUMAN TRAFFICKING IN REPORTING.

09/03/2026

Accountability and transparency that’s what Malawi need

08/23/2026

Mipingo moti sikudabwaso? Bola alandila. Judge winawake wanena zanali kuti Mipingo ili ndi udindo omafunsa komwe kwachoka ndalamazi. Apulezident 5 mita, minister 40 mita,, aaaaaa come on. Mipingo ikulimbikisa uchigawenga koopsa. Ndipo chifukwa chamipingo katangale a kukula msikhu

08/23/2026

Achina Kamangila wamisala , wansanje mwasewera bwanji?

Mukatero muziti Kamangila akupenga. Ndiye kupenga kwake mkwabwinotu. Lero onani wamisala uja nkhondo anawoona ija ili mtika.

Boma lapenga ngati Kamangila, ladabwa ndi money laundering. RBM yapenga ngati Kamangila. Amalawi onse ngabwino kuposa Kamangila and RBM is this 👇 Kamangila? It’s Reserve bank right? Koma Kamangila Sakhalin akukuwa? Inu nkumati ndiwamisala? Lero mumupepesetu

08/22/2026

Rule of law ndikanyama kanji? DPP singapange zimezo nthawi alibe

Photos from Pido International's post 08/18/2026

Hon Minister Ben Phiri, Ward councilors and members of parliament, learn something from Dedza Diocese.What you are using for a classroom block others have managed to use the same amount to build a full primary and two houses ie 90000 euros 180 million malawi kwacha. If we replicate this project means we can build 200 classrooms or more using Part of 5 billion cdf.

Same as, mlatho wa ku zomba kwa Mponda bwino uko, phungu wakana kuti bridge singapangidwe renovated using 1bilion kwacha, pomwe it costed 2 80milion kwacha. Akuti kutereko ndi kuba.

08/18/2026

Now you see the power of cartel?

When cartel wants you, patani patani amakuyikapo. Lero ndi zomvesa chisoni chaka chikutha without DG ku bungwe lalikulu ngati ACB, if Malawians were srs ndi kuthana ndi katangale izi anakakwiya nazo. Since DPP into the government, point chomwe ACB yapanga or choonesa kuti Ali ground? They are controlled by cartel, as they are controlling president.

Today you're saying all the candidates failed ma interview, are you joking? What kind of DG do you want? You're happy having no DG at ACB, because no one will hold you accountable. Izi nzokwiyisa

Photos from Pido International's post 08/17/2026

Scorchers taught us to be united. During the tournament, kunalibe wa UTM, DPP, MCP AND OR UDF. Tonse tinali amalawi support one team and one goal of winning the trophy. Football united us, and let's take a lesson.

Mr president , Mutharika mukulalikira za unity, but ur doing opposite of ur words. Konzani ubale wanu ndi JANE ANSAH. That will be a good example of unity. Let's united and be one Malawi. Let's build our home Malawi with unity. Arthur Peter Mutharika

08/14/2026

Because it involves you it's not a crime, but when it involves others it's now a treason?

08/13/2026

Akuti big fish, ena akuti ndima ministers, ena akulu akulu aboma, meaning namiwa uja samakunamizilani? We want details and names. After exposing them, we need arrests. Kumangidwa amangidwe. Malo amenewo agawana kuti? And who authorised? Musamatimate phula mkamwa kuti muzitisewera

Tikudikila so mwachete to see or hear kuti 9 officers from ADMARC has arrested. Panopa we are recording onse opalamula kuti amangidwe akayankhe, ngati sakumangidwa pali ganyu ife tiyigwira mpaka timve choonadi kuti who is shielding them.

08/06/2026

It pains me alot, it must also for you too.

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Manchester?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Manchester, NH
03103