Jigga583

Jigga583

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Jigga583, Health/Beauty, 234, Akasia.

19/08/2024

Lero ndifuna nding'alure wokwiya akwiye koma amve ndithu:

* Ngati mkadzi wanu akupanga zinthu 5 izi ndiye kuti siwanu ndipo ngati Pali mpata msiyeni palibe vuto.

1. Ngati mkadzi wanu akadali kugawa number yake mwachisawawa kwa amuna ena. Mlaliki 9:10.

2. Ngati mkadzi wanu akuvala zovala zoti Inu mkumulesa koma amavalira ndicholinga Choti amuna ena azimuona siwanu. 1 Peter 3:3.

3. Ngati mkadzi wanu akumalumikizanabe ndi ma ex Ake ziwani kuti mtima wake ukadali kuwakondabe amuna akale aja. Yesaya 43:18-19.-- mau amati zakale zapita....

4. Ngati mkadzi wanu samakupasani ulemu nthawi zonse amakhalira mwano, ndiye kuti alipo mwamuna amene amampasa ulemu. Efeso 5:33.

5. Ngati mkadzi wanu amagawana zinsinsi za mnyumba mwanu ndi amuna ena ziwani kuti mkadzi uyo siwanu. Mkadzi wanzeru amasunga zinsinsi za mnyumba mwanu. Miyambo 11:13.

- zikomo kwambiri mkhale ndi mmawa opambana nonse🥳🥳🥳🙏

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Akasia?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


234
Akasia