Maziko a Chipulumutso
Chikhalidwe choyenera ana a Mulungu
Malo ano ndipamrne timayankha mafuso okhudza mabanja komaso zimbwezi za chiyembekezo maka kwa achinyama,chomcho ngati mukukumana ndi mavuto amtundu uliwonse pa banjapo,bwerani tiwuzeni ndipo pano muthandizidwa ndipo mukhalaso pa banja labwino,ubwezi wabwino,kuthetsa banja si solution yothana ndi vuto mukukumana nalo,dziwani kuti vuto ndi mtimaaaaa!ndiye pano pali malangizo abwino,inu tulani nkhawa zanu basi
This is a page where we answer the questions,give the tips of how to have the good relationship with your partner more especially for the youths,so any kind of problems that you face in your relationship, don't hesitate, bring it,we are here to help,you don't have to leave your partner or betray and cheating on him or her no,he or she will change,good advise is here,thank you
2 Akorinto 13
5 Tadzisanthulani nokha kuti muone ngati muli mʼchikhulupiriro; dziyeseni nokha. Kodi simuzindikira kuti Khristu Yesu ali mwa inu, ngati si choncho mwalephera mayesowa?
Fuso nkumati,,kodi mungadziwe bwanji kuti muli ndi Mulungu?Awa ndi ena mwamafuso amene mpingo ukuyenera kuyankha,tiripano kuyankha funso lililonse limene inu mumafuna mutapeza yankho,dziwani kuti ofusira ndamene amakafika
God bless the works of your hands Amen
Mulungu amalemekeza chisankho cha munthu,kuteloku uli ndi ufulu ovomera kutembenuka mtima kapena kukana,Mulungu sachonderera munthu,chimene amachita ife ndikukakuponya kumalo okuyenera ukafa. Make your choice right now wisely
Mkazi alingati mtapo uwumbira mbiya m'manja mwa owumba(mamuna).Mamuna amapanga mkazi kukhala mmene iye afuna kuti akhale.
Bodza ukalimva kwa nthawi yayitali limasanduka choonadi,ndikunena pano ena muli m'mavuto chifukwa cha mabodza amene ena anawasandutsa chilungamo kuti iweyo ukhale pavuto basi
I asked another drunker to tell me what he can choose between beer or a woman?He said to me,beer is best🤔it's when I realized that 95%people choose to Sin becouse Sin is too sweet
The simple answer of the question, "what is to repent?" is:TO CHANGE THE MIND.From the beginning of your life in this world, Satan has been directing you to do his will,so when you submit your life to Jesus, simply means, you will no longer directed by Satan and you change your mind and allow Jesus to be your DIRECTOR.The question is who is your director?
When we say Jesus is the Lord and saviour, which means He save some one from something, if He is your saviour as well, what did he save you from?
John Baptist said, I am baptizing you with water, but the one to come will baptize you with Holy spirit. To be baptizing in water doesn't qualifys you to be Christian, you can lie to your pastor or who ever want to baptize you,pretend like what ever you say you will do,no one knows someone's thoughts, only God do,thank you Father you knows me than anyone do.There is no room in you that God can't opens and see what you hide, that is why oly Holy spirit qualifys you to be Christian.Repent now and be baptizing with Holy spirit. Amen
Click here to claim your Sponsored Listing.
Contact the business
Telephone
Website
Address
57 Pluto Street Plumstead
Cape Town