MANZY SA

MANZY SA

Share

NTHABWALA

20/10/2021

Eee koma ku mudzi anakoza amagulitsa Nkhuku kuti agule ndiwo

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

20/10/2021

Kukana chibwenzi mamuna okwatila kuli ngati kukana mabungwe opeleka chithandizo

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

20/10/2021

Mwana wako wabwela ndi homework, Iweyo wamuthandiza homework ija kenako wakachongetsa ndikukhonza zelo aphunzitsi ndikumuuza kuti mmawa ubwele ndi makolo ako😁😁😁

Muli inu ngati makolo mungapite?

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

13/10/2021

Osaonesa mtima onyanyalaπŸ˜‚ Dzukani phodani muzikaopseza anthu town

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

13/10/2021

Kod azimayi simungatsegule sukulu yophunzisana malilidwe?πŸ™ˆπŸ™ˆ alamu anu akumatchula maina anthu okufa kuno

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

13/10/2021

Ndimati ndikuuzen kuti Malangizo aja ndawayiwala ndiye mundilangizenso kena

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

12/10/2021

Anthu ena akamakuuza kuti ndakutuluka ngati uwafuse kuti kod inuso munali mwa ine?

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

12/10/2021

Mongokumbusana achina ndibwela December mwasala ndi mwezi umodzi okha
πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

12/10/2021

Mpaka pano sindimamvetsa Why nsuzi wa nkhwani umanyenya mbamu?πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”

πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”πŸ˜”

12/10/2021

Munakwatira mwachangu dala cholinga ife tikama njoya muzitivutisa ndi malangizo😏😏

Zichepe zimenezo muzipanga za banja lanu

😑😑😑😑😑😑😑😑

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Durban?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Queen Street
Durban