Anthu Akumbuyo
ndife anthu omwe tinakwera Kumbuyo kwa Bus
e
paja Anaphonya Yamikani Chester or Adadi a Professor Mnthalika Akhoza Kuchinya
anthu Akumbuyo akuyankhura zinthu zambiri
koma mkuti Senegal mpaka 70 minutes ndi Zimbabwe yomweyi osachinyako?🤣🤣🤣🤣
anthu Akumbuyo Ayamba kuseka Sopano
Kutani Waka Mkapangiske Vaccine 💉 uko Uzeleza apa
mwanyake Mkut Pala Wapangiska Vaccine ndikut wakana Chiuta AAAAAA Chindere iwe kwene pa Wanakazi maso mchanya aposo ndikut mwakana Yehovatu
Nde mwati pa Ulendo wathu waku Kenaniwo panopa tili chapati?? ndikare Tidanyamuka
anthu akumbuyo atopa
Man Utd fans: Tikupita pa Mwamba pa Arsenal tikasewera ma game athu
Yesterday
Man U 0-1 Wolves
Anthu akumbuyo: Vuto lanu mumaona Ngat Arsenal Anachita kuiponyapo
Full-time
Rwanda 3-0 Guinea
"Awatu tikawaponda ndithu"
anthu akumbuyo kuipasa Moto
Man Utd 0-1 Wolves
Anthu akumbuyo Atutumuka
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Cosimosty
Johannesburg