Buleya spots

Buleya spots

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Buleya spots, Health/Beauty, Richmond, Pietermaritzburg.

29/07/2022

MAWA LINO KULI KANTHU PA CHILIPA GROUND

OLEMEKEZEKA SHADRECK NAMALOMBA
K1MILION TROPHY

SEMI FINAL
MWAYA 1911 VS MPASA
CHILIPA GROUND
NTHAWI YA 2:30

ANTHU ONKHALA KU NAPELI, MATENJE, BLACK, MALENGA, NAUNJE, GOLAYE, CHIWAMBALA, NDI MADERA AMBILI TIYENI NTOSE TIKAKUMANE KUMENEKO

UTHENGA UMENEWU KUCHOKERA KWA KIMU RASHA KUCHOKERA CHILIPA

PANGANI LIKE PAGE IMENEYI KUTI MUZASATILE MASEWERO AMPIRA

22/07/2022

TNM SUPER LEAGUE
IKUBWELERASO GROUND MAWA LINO

19/07/2022

2017 FIST ROUND INALI NTCHOCHI PAKA MANOMA ANATENGA KATUNDUYO
KODI CHAKA CHINO ZICHITIKASO

KULI KANTHU WEEK INO PAMENE TNM SUPER LEAGUE IKUBWELERASO BWALO.

19/07/2022

TNM SUPER LEAGUE
TOP GOAL SCORERS

18/07/2022

PENA MOYOWU TIZIGANIZILA KUTI TSIKU LINA TIZAFA

panali banja lina limene linali ndimwana modzi wamuna.
Mwanayu anali wa man Khalidweu abwino paka pamene amakula chifukwa chocheza ndi azake amene anali olowelera. Anayamba pang'ono pang'ono kusatila makhalidwe azake aja.

Moyo wake pang'ono ndi pang'ono unayamba kulowelera kuyamba kumwa mowa makolo ake anali akumulangiza za Khalidwe lake loipayo koma amangowavomera koma zinali zovuta kusiya chinthu chimene amachiwona kuti chabwino pamoyo wake.

Anali kupitiliza Khalidwe lake paka anayamba kuba makomo ayinuwake zomwe makolo ake anali akumulangiza za Khalidwe lake kuti tsiku linalake azagwidwa kumenyedwa mosankhala bwino koma yeyo amawona kuti zovuta kusiya chifukwa anazolowera.
tsiku lina anapita kumudzi wakutali kwambili ndi kwawo kokaba mwasoka anagwidwa ndiye kunali kumenya inu anthu munthu kulephera kupepesa koma anthu osasiya kumenya munthu kulira kufikana potopa pamapeto paka munthu anafera pomwepo

chimodzi modzi moyo uno anthu sitikuna kulapa machimo anthu.
chinthu chomwe tikuchikonda masiku ano chimene mawu a mulungu si chololedwa timawona ngati vuto kuti tisiye chuma chanthu chomwe tinachipeza munjila zosavomelezeka pamaso pa mulungu. Tikukonda zinthu zomwe zili zokanisidwa malemba a mulungu koma munayamba mwaganizapo kuti tsiku linalake moyo muli awowo azaufuna munuwake okulengani muzankhala mu kulira ndi kukukuta Mano poganizila nthawi yomwe mukawononga muli pa dziko pano osayigwisa ntchito bwino.

Mukhale ndi tsiku lopambana ambuye akudaliseni

18/07/2022

Anthu aku Dedza amakonda team yawo amayipasa molaro kwambili

18/07/2022

TNM SUPER LEAGUE
IKUBWELERASO WEEKEND IMENEYI KULI KOKEKOKE SABATA INO

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Pietermaritzburg?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Richmond
Pietermaritzburg