Devorced men and women
Dear friends lets sharing idea here about devorced ones
Nonse mphere mumadzidziwa. Funso langa nali: kod okondedwa wanu ali ndi mphere zija zochita kumatuluka magaz ndi mafinya zija mungamagonebe malo amodzi nkumafundabe chofunda chimodzi?
Mabanja apa jonz mamuna 25 years nkazi 38 years ankhoswe 19 year. Ayi dzikomo mwafasako
Nginjili chi 200,000 ku account kwanu. Pompo X wanu akuimba amvekele sorry ndimafuna ndiwatumizile masten chonde its a mistake ndibwezele ndramazo, muli inu mungatani? Azimai yankhan m***a.
Inutu bwenzi mutakwatiwa kalekale koma vuto mumatchena ngat muli pabanja kale
No matter how a girl love her boyfriend, but she still have another boyfriend
Osaononga ndrama kukaedzesa mimba ndi wachikondi wanu, ingotendani bisiketi nkulowesa kundata ngt simuiona pakatha ma minutes angapo ndie k*t mwana waidya
Azimai osanyoza chingwe chokokela madzi k*ti mchachifupi vuto chimakhala k*t chisimecho mchakuya kwambiri
NGATI CHIBWENZI CHAKI SICHIMAKUPEMPHA NDALAMA MUTAYE CHIFUKWA ALIPO YEMWE AMAMPASA
Kod ndibwino kusunga mankhwala ophela tizilombo toononga mbeu mnyumba mwanu?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Ntapwa Primary School Box 54 Ntaja
Pretoria