kapyola SD
Personal blog
27/02/2026
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL .S. BANDA.
____________________________________________
Progress!
Masalimo 84:7
"Iwo amanka nakulirakulira mphamvu"
30/01/2026
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL .S. BANDA.
_________________________________________
Lions Lacking But The Children Satisfied
Masalimo 34 :10. Mikango itha kulefuka ndi kumva njala koma iwo amene amafunafuna Yehova sasowa kanthu kalikonse kabwino.
16/01/2026
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL .S. BANDA.
____________________________________________
“Voices Amplified and Exploits Ignited”
1 Yohane : 2 :14
...Inu anyamata, ndikukulemberani chifukwa ndinu amphamvu. Mawu a Mulungu
amakhala mwa inu
ndipo
mumamugonjetsa woyipayo.
02/01/2026
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL .S. BANDA.
_________________________________________
New Year's Blessings![Perfection, Establishment, Strengthening, Settling.]
1 Petro 5:10
Ndipo Mulungu wa chisomo chonse, amene anakuyitanani ku ulemerero wake wamuyaya mwa Khristu, mutamva zowawa pa kanthawi, adzakukonzaninso , adzakhazikitsa ndipo adzalibikitsa inu pa maziko olimba.
19/12/2025
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL .S. BANDA.
___________________________________________
Faint; but not Faint-Hearted
Oweruza 8:4
Ngakhale kuti anali otopa anapirikitsabe adani awo.
21/11/2025
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL .S. BANDA
___________________________________________
Questions Which Ought to be Asked
Yobu 35 :10-11
10. Koma palibe amene akunena kuti, ‘Kodi ali kuti Mulungu, Mlengi wanga, amene amatisangalatsa nthawi ya usiku,
11. amene amatiphunzitsa kupambana nyama za dziko lapansi ndipo amatipatsa nzeru kupambana mbalame zowuluka?’
31/10/2025
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV. DR. DANIEL.S. BANDA.
__________________________________________
THE ANXIOUS INQUIRER
Yobu 23:3
Ndikanangodziwa kumene ndikanamupeza Mulungu; ndikanangopita kumene amakhalako!
24/10/2025
Zambia, Independence Day can serve as a time to reflect on the blessings of political freedom and the responsibilities that accompany it.
It is an opportunity to give thanks for the liberties enjoyed and to pray for those who are still under oppression.
Moreover, it is a reminder of the greater freedom found in Christ, which transcends all earthly circumstances.
Happy Independence Day!
17/10/2025
FRIDAY EVENING GEM 💎 WITH REV DR DANIEL .S. BANDA.
_________________________________________
The Main Matter
Yohane 20 :30-31
30. Yesu anachita zodabwitsa zambiri pamaso pa ophunzira ake zimene sizinalembedwe mʼbuku lino.
31. Koma izi zalembedwa kuti mukhulupirire kuti Yesu ndi Khristu, Mwana wa Mulungu, ndi kuti mukakhulupirira mukhale nawo moyo mʼdzina lake.
09/10/2025
Be there!!
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Chipata
Chipata